Andre Charles

Andre Charles

Share

ANDRE CHARLES

20/05/2026

Abale athu adzakhala abale athu mpaka kalekale. Tisamanyoze kapena kuiwala chibale.

1. Tiphunzire kumasunga chibale.
2. Mukapeza mpata, ayendereni abale anu; ngati ali k*tali, ayimbireni phone.
3. Mukakhala ndi k*thekera, athandizeni abale anu.
4. Mukasemphana, yanjanani nawo mwamsanga.
5. Pewani nsanje ndi chidani pakati pa abale.
6. Tizipemphererana ndi kulimbikitsana nthawi zonse.

“Taonani, n’kokoma ndi kokondweretsa k*ti abale akhale pamodzi mwa umodzi.” Masalimo 133:1

19/05/2026

Kodi iweso et

19/05/2026

Nzanga wamuthaa pep

Kagwiree🤣🤣🤣🤣🤣

19/05/2026

Si Basi Arsenal are Champions of England???

Congrats ma Gunners

Photos from Andre Charles's post 19/05/2026

KUCHOKA NEXAHELA KWABWERA NOVACASH iyi ndiye ili bho
registration fee ndi K14,500
Kuliso spin,amakupasa kamoz ulele kwnako umalpla(Spin imeneyi ukalingna nayo umatha kugwira 20pin)

link and guidance 0880256508(WHATSAPP)

19/05/2026

Ngati Yesu sabwera zaka 100 zikubwerazi ndye k*t tonse tizakhala tamwalira

18/05/2026

Titulutse liti imeneyi

17/05/2026

17/05/2026

kumakhala bwino ndi anthu za mawa siximaziwika

15/05/2026

SONG
CHARLES

15/05/2026

Olo musapange like bola mwaona 😆

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Rustenburg?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Rustenburg Noord Burn Street 30
Rustenburg