Mwayi chaola
Stories
Hie guys
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Blunk T Danso Refuji, Ireen Mumba
05/06/2024
Still in stock @ good price
Ndabwerako🙌 ndikapena baibulo yamu 4n tiyamba kugawana uthenga
Nyengo yasitha Moyo wasitha.. Ife Ambuye mutitsogolere tisasithe.😭
Papita thawi osapezeka pa page imeneyi pano ndabwera panali vuto lakusowa kwa baibulo lamu 4n
Zikomo Yehova pondipasa Moyo ndili nawowu🙏
Kusowa Kwa zakudya komaso zamoyo padziko lapasi... ndchyambi chopangsa Satana kubwera ndmzeru zake.feteleza ndnjra imodz yokopela anthu za ubwno wake koma tikat tiwone nd njira imodzi yowonengeraso thaka yanthu ndpo Malo omwe pagwilitsidwa feteza kwambil chomera sichilongosoka ngat smuthiraso wina...relo akusowa ndpo tikudana nd tsogoleri pot ndamene akuchedwetsa ndkuwuzen..masiku antha tsopano...dziwan k*t ifika thaw yomwe muzawone chilchose chkhale moyo zkulira makhwala a science... Khuku zomwe tikudyaz Pano zimabayidwa makhwala k*t zkule mwachangu zomwe zkusonyeza k*t anthuwa akupanga zamzeru koma osazwa k*t ndnjira imodz yowonongera znthu ndpo idzafika thaw yomwe sitidzachitira mwina koma kuvomeleza m'bale relo lino lapani popeza anthufe thaw yowawa yatsala pang'ono ndthudi
Daily timagona ndkupumisa thup lanthu... Koma daily tikagona timaiwala k*t chilchose Chitha kuchitika pepherani🙏
Ku dziko la Britain
Mzungu wina analowa mu restaurant. Atalowa, anaona munthu wakuda atakhala pa corner pa restaurant yo.👨🏾
Mzungu uja anamuitana opereka zakudya kenako anakuwa ak*tulutsa mpuk*tu wa ndalama zake amvekere..."Ndimugulira aliyense zakudya muno!! Kupatula munthu wakuda wakhala apoyo!"
Opereka zakudya uja anagawa zakudya kwa anthu onse mu restaurant muja kupatula munthu wakuda uja.👨🏾 Mmalo mokhumudwa, munthu wakuda uja anamuyang'ana mzungu uja kenako anayankhula k*ti.."zikomo".
Izi zinamukwiitsa mzungu uja ndipo anatulutsa mpuk*tu winanso wa ndalama nakuwanso k*ti..."Ndimugulira aliyense botolo la chakumwa chilichonse chomwe akufuna muno kupatula mkada wakhala apoyo"👨🏾
Opereka zakudya uja anagawa zokumwa restaurant yonse kupatula munthu wakuda uja👨🏾. Munthu wakuda sanadandaule kanthu koma anayankhula mawu ok*ti.."zikomo".
Izi zinakwiitsa kwambiri mzungu uja, ndipo pompo anamuitana opereka zakudya uja k*ti amufunse funso. Atafika opereka zakudya, mzungu uja anamufunsa k*ti..."Kodi munthu wakudayo vuto lake ndi chani? Ndagulira aliyense chakudya ndi zakumwa muno kupatula iyeyo, mmalo moti akhumudwe akungosekelera kenako nkunena k*ti zikomo. ndi wamisala kodi?"👨🏾
Opereka zakudya uja anayankha nanena k*ti..."Ayi siwamisala. Iyeyo ndi mwiniwake wa restaurant yi"
Phunziro: Adani anu azakugwilirani ntchito yokomera inu koma iwo asakudziwa k*ti ak*tero.😊
Clique aqui para solicitar o seu anúncio patrocinado.
Categoria
Telefone
Website
Endereço
Songo