Nitrix Matama

Nitrix Matama

Share

Official Page of Nitrix Matama |
a Malawian Rapper πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό| Songwriter | Multiple Award Winner koma kumaloto eti Artist

25/04/2026

titha kungoimbira Peer pressure πŸ˜‚
Chidolo ichi tituluse nyimbo avine et?

25/04/2026

Ka chips aka 5 a mwayi ikamati 1bar alandiraosaponya ndikulowera inbox
❀️

24/04/2026

ALUMVAIMVA mazembera ine nanga inu mmavala Jombo komabe imandiwaza hvy link πŸ‘‡

22/04/2026

Malangizo Aras ndawaponya kunkhongo zituluke iwe ukuona bwa?

18/04/2026

Zija amanena EvanzMuzik zija adha awa apeleka maganizo awo inu muona bwanji?

18/04/2026

Ndinapanga post list ya nyimbo zomwe ndikufuna nditulutse kenako awa mkuzalemba IziπŸ‘‡πŸΎ guys ndizoona Izi???

Kusatulutsa nyimbo kwa Chaka ndinasunthapo wezi makagwila ntchito zina zaboma so I was very busy oti sizikanatheka kumatulusa nyimbo since ukatulusa nyimbo zimafunika kuipanga follow up so yeah koma apa am around and Ma busy anga athaaaa

Tiyambepoooo!
TeamMatama

18/04/2026

1. Aras reloaded ft S khrizy
2. Ndabalalika
3. Moto ft Bandera Wachiyawo & K Millz
4. Picture yako ft PST (Zambia)
5. ……….ft wikise

Tiyambe iti???

17/04/2026

Muzonse kumathokoza
anthu tikuchoka kutali πŸ™β€οΈπŸ™

15/04/2026

nazo boyfriend kuvala ngati Gule waku 36 πŸ˜‚πŸ˜‚

15/04/2026

kod timayenera tizivala chonchi et?

12/04/2026

HELLO PIPO ituluke liti?
mwadikira kwakwana
πŸ”₯πŸ”₯

11/04/2026

APA ndiye ndakudulani Mutu
Ndipati ? πŸ˜‚πŸ˜‚

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Area 23
Lilongwe