WORLDstudios
Music production
08/01/2026
Mayi wazaka 38, Esther James, amugamula kukakhala ku ndende zaka zisanu ndi chimodzi kaamba kopezeka olakwa pa mlandu othyola ndi kuba katundu m'nyumba wa ndalama zokwana K149,000.
Bwalo la milandu ku Lilongwe ati linauzidwa kuti mayiyu adapalamula mlanduwu mu April m'chaka cha 2024, ku Area 36 munzinda wa Lilongwe.
Malinga ndi mneneri wa polisi ya Lilongwe, a Hastings Chigalu, maulendo atatu onse, mayiyu anathyola nyumba ya mayi wina ndikubamo katundu osiyanasiyana monga sugar, mafuta ophikira, zitenje komanso matilesi.
Olemba: Catherine Banda, Lilongwe
copied...
03/01/2026
coming soon π¨
taverako pang'ono koma ππ₯
Chaka chikutha samalan abale π
08/12/2025
Manchester United apapa yabwela Kell Kay ππ£
05/12/2025
https://youtu.be/zwtx24tbo2c?si=46EzOpXyKyoG-mTI
Afana Ceez π
Afana Ceez - Zinthu (Official Music Video) Directed by Seany films & Praise UmaliPerformed by Afana Ceez Guest appearance by Ching'aning'ani
Sunday labwino kwa nose π
26/09/2025
Phyzix udolo wako unasefukila pano ophweketsa ose aja amakufunila zabwino kuli mulungu kunjaku ππ
26/09/2025
hip hop kugundana mitu π΄
Gwamba
Olivia Media. Mikozi ππ zaone nkhondo kuno
Chakwera was chasing me in my Dream immediately i shouted Mutharika and he disappearedπ
The MCP, UTM,PDP, and UDF are expected to hold a joint press briefing today in Lilongwe.
Follow WORLDstudios π
19/09/2025
Tiponya ka fanta osadanda π€π
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Chingwiri
Lilongwe