Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia

Share

We are Professionals in TV/Radio Adverts, Documentaries, Film Production, TV/Radio Programs, Graphic Designing, HD Photography, Screen Printing and many more.

We are Affordable with Best Quality.

06/06/2026

Andy wa Chisomo,
Happy Birthday mfana.
Matonde mulangizeni munthuyu

06/06/2026

Inunso muli nawo mugulu lopanga Magic Swap? Ndikudabwatu.

Photos from Nkhalango Multimedia's post 06/06/2026

Eeeeeee Koma tiwona zinthu,
Inu mwadziwa zoti lero kuli Birthday??
Nafenso tangoonera zithunzi, ndipomwe timafunsana kuti kodi ndi Ai?

Mhu! Gaga Pachema Munyanyiwa waulumikizatu ulisi ngati munthu munthu.

Happy Birthday Munthu wa Mulungu, oyankhulidwa kumaloto.

05/06/2026

Top fan pano Patuma Tonex mawa akukananala ku banja pheee, ma Tonde ndi ma 40 mpatseni moto komanso muuzeni kuti mawa mpunga wanyama tikadya nawo

01/06/2026

Tikupelekereni moni kwa ndani??

31/05/2026

LA 40 lamukwanira,

Francis Magome, amutapa chifukwa Chotsegula Private Clinic komanso kupezeka ndi mankhwala opanda chiloledzo ku Chikwawa.

31/05/2026

Shakira wakana Gawoni ati siokonzeka kutenga Mimba

30/05/2026

Zakhalanso bwanji?

30/05/2026

Half Time
PSG yaumohawi 0
Arsenal Champions 1
Koma timwa madzi?

30/05/2026

Mike waona chani mwa Shakira abaleeee?

Want your business to be the top-listed Media Company in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Limbe
Blantyre
MW