Oracle visual
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Oracle visual, Digital creator, Kamhlushwa, Nsanje.
27/03/2026
Lero tinali kumma office a home affairs kukasayinila ma pepala a ID yanga ndi madam Aku nyumba😍
Koma nde pojambulitsa ID kudzayipha style koma eti akaniza akuti kuno zimenezo ai🤣🤣🤣
27/03/2026
Chimene mumafuna inu akazi mudzachipeza ndithu ati ali kopangitsa surgery Nyash🤣🤣🤣
26/03/2026
Nanga tizisalira Nafe tiyeleko basi Kukhala okuda ndikufuna Ishaa!!!
Atero Mayi Caro Mpaka kulandila kiti yonse yaku company 🤣🤣🤣
26/03/2026
Ati "ndizamusintha ndekha" ungasinthe Hule waku Lunzu iwe?🤔
😂🤣😆💔💔🙌🙌
26/03/2026
Ku Chikwawa Bambo wina Amadwala kwambili ndipo Matenda ake Anali akachibweleza bweleza kuchila lero mawa adwala ndipo Banja lake limakhala la nkhawa koma iyeyu anati musadandaule ndikhala bwino.
Pakutha kwa masiku bambo aja anayitanitsa mwana wao womaliza ku badwa ndi Nkazi wake kumuuza kuti Ngati angamwalire Bokosi lake lidzatulukile Pa kona la nyumba lake ndipo mwana wake ndi mkazi wake anagwidwa ndi mantha koma anati nabola ndanena.
Ndipo zina chitikadi atamwalira mwambo unayenda moteromodi ngati mene ananenela mwini wake.
Mwakuganiza kwanu mukuganiza kuti adakasephanitsa Zomwe anawauza Chidakachitika ndi chani?
25/03/2026
Pali funso apa musanagone
Kodi mungavomereze izi👇?
Osagonana kwa zaka 5 zonse mukakwanitsa
mulandira ndalama zokwana $4MILLION ,tikayisintha mmakwacha lthink NDI 7billion Ngati ndisakulakwitsa
Zaka 5 zopirira 🤐
Koma tsogolo lanu likhale losinthika moyo wanu
Kodi inuyo mungakwanitse?Nenani m***a mtima moopa mulungu
✔️ YES – Ndikuvomera, ndalama ndizofunika 💰
❌ NO – Sindingathe, moyo wa chikondi ndi wofunika ❤️
Tag anzanu tiwone maganizo awo 😄
25/03/2026
Akulu awa kwawo ndiku Chikwawa amugwila anthu Chifukwa amanyengana ndi Agogo ake mpaka awapatsa mimba izi zachitika pamene Anthu azindikila kuti gogowo ali ndi pakati.
Ndipo anthu atawafunsisisa anati ndi dzukulu wawo amene wapeleka mimbayo Ankachita Ngati kuwagwililira akatero ankawapatsa ndalama kukhala ngati Chiseka pakamwa,Ndipo anthu a mudzi akwiya ndi Nyamatayu Ndipo amumanga Ulendo naye ku police.
Cholinga chale sichikudziwika kuti amapangilanji zimenezi kapena Kukhwima Zosadziwika ndipo anthu amupana ndithu kuti ndi chifukwa chani amapanga zimenezi Ndi iyeyu Amangokhala chete osanena.
Zonsezi Mkati mkati mwa ulendo wopita ku Kenani 🙌💔
25/03/2026
Tsikana uyu Akuti amacheza ndi njonda inayake ndipo amafuna thandizo lake chifukwa amafuna ndalama kuti akagule zofuna zake.
Koma Chodabwitsa ndichoti Nyamatayo wangomusendela ndalama ndi Batile pamwamba pa ndalama ,Ndipo wabalalika Sakudziwa kuti Akutanthaunzanji Nyamatayo .
Muthandizeni Maganizo anu akufunika kwambili🙏♥️
25/03/2026
Azimayi ambili Amalowa Bafa akuyimba nyimbo,Kusamba Akuyimba Nyimbo koma Pamazafike pena pake amazasiya kuyimba Kodi amakhala Akuchita chani.
Kenako nyimbo ija imadzapitiliranso🤣🤣🤣🤣🙌
25/03/2026
After kuthandizila kupha mzimayi nzake ndikumasekelera afterwards, amumbwandila.
_________
Mtsikana amene anatchuka ndi chithunzi choyambiliracho ali mu zebra 🦓 dress wagwidwa ndi a police dzulo pamodzi ndi anthu ena ochuluka omwe anathandizila kupha mzimayi wa business emwe anamunamizila kuti anaba katundu wina obisika wa pa thupi la m’nyamata wina, later atamufufuza m’nyamata uja zinapezeka kuti ndi zabodza koma mzimayi anali ataphedwa kale ndi gulu, a police agwila anthu opitilira 200 pa nkhaniyi (allegedly)
25/03/2026
Situation ndi mmene ilili panopa mumzinda wa Durban.
Kumenekutu kuli magulu osiyanasiyana motsogozedwa ndi March and March Movement komanso Operation Dudula
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Culinary Team
Attire
Telephone
Website
Address
Kamhlushwa
Nsanje