SLYC
SLYC, real name Innocent Malemia is from Zomba city, Malawi, started his carrier in 2010
08/06/2026
Happy birthday To myself 🔥🎉zolangizana zokwatira Chaka chino ayi 😁🙌aliyense akuona mene zikukhalira pa mpanje pano..
07/06/2026
Tiyeni tivomereze kuti Mw ndi shasha eh 🔥
Fred Mw - Zepu (Official Video | Dir. M Feli) A New Music Video by titled "Zepu" Enjoy it ✨✨✨🎉🎉🎉 ...
07/06/2026
Birthday wishlist ndiyosaka 25sau nkagulire mpunga 1kg 3sau, squash 12 sau, ma parts a chicken 5sau, yosalayo tomato, spices ndi masamba, ndi 1sau ya mzimbe wokudya poyenda pochokera kogulako🔥😂🔥🤲 Zikomo🤝
Kmatu mw Nyimbo iyiyi nde ndiduka nayo mamama🔥 hane bwerani umvere👏😬https://youtu.be/QPAzB8ChG34?si=hrmSgQT55tX-hhAk
02/06/2026
Kale nnali mfana wabho 🤝🔥😂🔥 apa nnali nduchokera kumene kuJando😜
29/05/2026
Beat nde yakungidwa😁🔥, recording done🔥 kwinako ndingoti 👏
amen 🤲
Good morning 🌄🌞
27/05/2026
Kuphunzira kunyada😂 though mahopu 😂
Yesi aDah🤗😂🔥🔥🤝 I g*t the vibes😋🔥😬
25/05/2026
Plan ndiyoti ndikupatseni birthday present pa 8June kma vuto ndalama 🙌😬
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Zomba City
Zomba
7941