Timaphusha Talent
π¨TIPHUSHE LUSO From GHETTO to the World π MUSIC, MODELING, DANCING and so many ARTS ππ
22/06/2026
π― Meet BEAUTIFUL π₯°β€οΈ π²πΌ π₯ π―the only Malawian Content Creator yemwe anafikako ku NEWS nd content yake π₯ππΎ Zobhebha tu π€π
π Koma Apa π£οΈπ£οΈπ£οΈ eeeh πππΎπ
πKodi mukuti myambana chani kweni kweni K*t Chithe Chibwenz?π€·πΎββοΈπ€£ππΎ
19/06/2026
π NKHANI YA CHISONI π π
π£οΈ Mkulu odziwika bwino pankhani zojambula zinthunzi RAS PETER KASENGWA wamwalira atadwala mwa nthawi.
π£οΈ KASENGWA zana lapitali analemba pasamba Facebook kuti akudwala ndipo lero talandira uthenga ot WATISIYA ππππ²πΌ
π£οΈ Mzimu wa Ras peter kasengwa ukause mu mtendere.ππΎππΎππ
17/06/2026
π NDE Mwati Munamva ZOTANI za Akazi OTELEWA? Akazi a ubweya miyendo mu π₯°π ... Fukwa nde anthu amakamba zambiri tu π€£ kaya zoona nd zitiπ€·πΎββοΈ π³ππ
π£οΈ Inu Mnamva Zota..... π€·πΎββοΈ
π UPCOMING ARTIST HIT DM ngat Mufuna PROMO π€πΎπ²πΌβ
17/06/2026
π and MADNESS β¨ π₯ two young and Talented Superstars β¨π²πΌβ
π₯π€πΎ
π£οΈ UPCOMING ARTIST... BWERAN DM TIMVANE ZA PROMO π€πΎ π²πΌ π
17/06/2026
π Tsiku lomwe azakwitile MANYIZO kuzachema kwambiri eeh π€π nde akati awuluke Ulusi utha kuona ngat Chugwira BANK π¦ inayake m Town Mu π π₯π₯π«΅πΎ
π£οΈ Uyu nd DOLO β
HUSTLER β
RAPPER β
INFLUENCER π²πΌ π₯π
17/06/2026
π CHITHUNZI chi chinali mu Nyimbo yanji π«΅πΎπ³π³ TCHULA ngat Umasatadi URBAN MUSIC pa Malawi π²πΌπππ₯π«΅πΎπ€πΎ
π£οΈ UPCOMING ARTIST... BWERAN DM TIMVANE za PROMO π€πΎπ²πΌβ
17/06/2026
π MA PANZA PA TOWN π²πΌπ₯ππ
& BENSAM
17/06/2026
π MALUME afika kuchoka ku JONI nde akuti Anamusowa FANTA kwambiri π€£ π€£ π€£ ππΎ eeesh koma yaa nde kuluma tu π€£ π€£
17/06/2026
π INCASE you Missed β½ βΌοΈ π π
π£οΈ DZULO GOATED π π Messi wachinya ZITATU.... π Uyu nd Goat wa ena ndpo Lero kuli so Mpira WA GOATED π wina C. RONALDO π³π³π ππΎ Kwachema kwambiri π€£π€·πΎββοΈ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
City Centre
Zomba