Mezaneyo music
Music in ma veins
Follow Mezaneyo music
WEEK YANU INALI BWANJI? INAKUWAZANI KWAMBIRI NDI ITI?
1. Anyamata 8 afa ndimowa wa ambuye Tengeni tikunena pano akuyimba Hosanah ndi achina Ngelo Gabriel
2. Eid yachaka chino akhristu ambili ayidandaula kuti kunalibe zakudya zokwanira
3. Apule anakayendera apolisi atsopano omwe angomaliza Training yawo kumene Koma anthu ambili akhumudwa ndi ma telala amene akutsoka ma uniform awo.
4. Eli njuchi watulutsa album yomwe anthu ambili apeleka maganizo awo osiyanasiyana,ena akuti ndiyabwino ena akuti wangoyimba ngati wakakamizidwa kuti akhale relevant.
5. Oyimba wina amafuna kukhapidwa ndi achiwembu, wachita kupulumusidwa zikwanje zitayamba kale kunjanja pathupi lake, koma mpaka pano sichikudziwika chifukwa chimene anthu amenewa amafuna kumuphera.
6. Oyimba winawake otchedwa JB yemwe amakhala ku America watulutsa nyimbo yatsopano "VACATION".Nyimboyo ndiyabwino kwambiri koma yangovuta kuti intro sanailowe bwino,beat sinapangidwe bwino,ma lyrics salibwino, production silibwino, pronouncing yamawu silibwino komanso ikumamveka bwino ikakhala pa mute.Ena achipongwe mkumati wapangira record Toothbrush.
7. Kellkay ndi Yo maps atulutsaso nyimbo yatsopano over 218k views on YouTube in 2 days
8. Oyimba wa Gospel Gwamba yemwe waikidwa pa billboard ya betting company wapita Ku USA komwe Kuli IVLP conference.
9. Bullets ikupilirabe kuvutika mu league season ino pomwe yapanga draw ma game awiri otsatana.
10. JETU watola BMW pa City mall
Bonuses
- Chovala cha Saint ngati nthumbwana (ofals)
- Artist okanika kuyankha chizungu (kuyipatsa basi)
- Mutale Mwanza Outfit and English Fluent
- Nkhondo ya Israel and Iran
- MP wachikaladi
- Manchester United
- Ma Bosslady atatu Ku Epic
Akhalitse Malawi Mr Vakeshooooniiiiii ndiye Topic yathu ya week imeneyi.
Year0 ataledzera amvekere🗣️
13/04/2024
mezaneyo in Lilongwe mezaneyo in Lilongwe
God will make a way
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Malosa
Zomba
13/04/2024