DALI BEATS

DALI BEATS

Share

β€’ Producer 🎹
β€’ IT Expert βŒ¨οΈπŸ’»πŸ“±
β€’ Song Writer πŸ“
β€’ Lover β™₯️
β€’ Joker πŸ˜‚
β€’ Movie Talker πŸŽ₯

14/03/2026

GOOD NEWS!
Kuyambira lero mpaka mtsogolomu, you will now be able to stream and download my free instrumentals on your favorite website

Enjoy! 😍

https://share.malawisongs.com/song/2OqioHnYFvyU?UI=share&SrcWeb=malawisongs

24/02/2026

Nde Kwagwa Muliri Wa Ka App Aka EeehπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ™Œ

Photos from DALI BEATS's post 21/01/2026

AKUPEMPHA THANDIZO LA NKONO WA PULASITIKI-CHIMOMBO

A Maliko Chimombo azaka 38 ochokera kwa Kachere mfumu yayikulu Machinjiri ku Blantyre akupempha thandizo la nkono wa pulasitiki omwe umawathandiza kugwira ntchito zina ndi zina.

A Chimombo ati nkonowu usandaonongeke amakwanitsa kulima komanso kugwira ntchito yoyendetsa njinga ya kabaza koma zonsezi zidaima.

Iwo apempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize ndi mkonowu kuti azitha kugwira ntchito zoti azitha kuzithandiza moyo wawo wa tsiku ndi tsiku komanso akupempha thandizo la ndalama zokwana K700, 000 kuti ayambire bizinesi ya golosare.

Anthu onse akufuna kwabwino atha kulankhula nawo pa : 0996953732

Wolemba: Cynthia Mpofu

13/01/2026

Guyz, What is transport to Lilongwe to Blantyre? I am go to interview😌😊

13/01/2026

Inu ma chief editors pali ma 2pin, tapangan zantchito..tikufuna uvuni apa tiwaonetse eni; dollar tinadya kale😫😫

11/01/2026

0885 42 60 01
For Business/Booking

10/01/2026

Inu mwaziwapo ndani apa?🀣🀣

09/01/2026

Artist wanu ujaπŸ˜‚πŸ˜…πŸ™Œ
Chonde osamupanga tagπŸ˜«πŸ˜‚

07/01/2026

GOOD MORNING! TABELEDWA IFEπŸ˜”πŸ˜­

Aliyense amene analowa m’nyumba mwanga ndi kuba ndalama, ma phone awiri (Smartphones), zovala, laptop ndi desktop yomwe ndimapangila za studio, munaiwala foni yanu pa tebulo.

Ndikudziwa kuti ndinu ndani, ndinalowa pa Facebook yanu ndipo ndaona nkhope yanu.
Muli ndi 24hrs yokha kuti mubweze katundu yense komanso mukonze chitseko. Mukalephera, ndidzachita zomwe ziyenera kuchitika ine za police sindipanga nawo

Account ya Facebook yanu yasiyidwa pano kuti aliyense adziwe
πŸ‘‡πŸ‘‡

https://www.facebook.com/profile.php

05/01/2026

Pov: Me trying to explain why I do not have money in January πŸ˜‚πŸ˜…
Add yours in the comment section πŸ‘‡Best comment with more likes wins MoFaya Weekly bundle

03/01/2026

Ntchito zina eeh πŸ₯ΊπŸ˜‚πŸ™Œ
Uyu ndi onenele fodya uja πŸ˜‚

03/01/2026

Ku Zomba nakoπŸ€£πŸ˜‚πŸ™Œ
For the love of Apple πŸ˜…

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Zomba