Ghama
Rest if you must, but donโt quit. Daily hidden motivation | Real life wisdom | Hope for the struggling. Note: Ghama is an Artist inside the Creative World.
Some truths are hiddenโฆ follow to discover what most people never see.
20/08/2025
Ghama, Imozi mwa nzika yokhuzidwa ndi mene Malawi alili lero๐.
As a Nation, all of us ngat amalawi tikuyenera tidziwe izi.
Dziko lathu lokondedwa likukumana ndi mavuto a chuma osaneneka. Mitengo ikukwera tsiku ndi tsiku, ndalama yathu ndiyogonja, mafuta ndi mankhwala zosowa, ndipo mabanja ambiri akuvutika kuti apeze chakudya๐. ngakhale zili chonchi chiyembekezo chathu chisatithawire, chifukwa mitundu yayikulu imamangidwa osati pa nthawi ya mtendere, koma pa nthawi ya mavuto pamene atsogoleri ndi nzika zimayima limodzi ndi kulimbikira.
Ngati Malawi tiyenera kuyima molimba ndi mokhazikikanso, tiyenera kukhala ndi utsogoleri wolimba mtima, boma loona ntima komanso mgwirizano wa anthu onse.
njira zomwe zingatithandize kuzitolera ngati dziko
1. Kukhazikitsa chuma. Boma likuyenera kulimbana ndi kukwera kwa mitengo, kuletsa kubwereka ndalama mopanda malire, ndipo Reserve Bank iyenera kugwira ntchito molimba mtima komanso moonekera poyera. Anthu ayenera kuwona mmene zinthu zikuyendera mwezi uliwonse.
2. Kukonza nkhani ya ndalama zakunja. Boma likhazikitse msika wowonekera bwino wa ndalama zakunja, kuyika patsogolo mafuta, mankhwala, ndi feteleza kuti amalawi asamazinzike kamba ka kusowa kwa izo.
3. Kumanganso chidaliro ndi anzathu akunja. adziona okha khalidwe labwino, Malawi adzapeza chithandizo even kuchokera ku mabungwe monga IMF ndi World Bank. Komanso thandizoli lisathere matumba mwaanthu ochepa adyera, koma kuthandiza osauka.
4. Kukhala ndi chakudya khomo lililonse. Palibe mwana amene ayenera kugona ali ndi njala. boma kuonjezera thandizo la chakudya kwa osauka, kulimbikitsa ulimi wa nthilira, ndi kubwezeretsa nkhokwe za chimanga motsogoleredwa bwino komanso kuzipanga poyera.
5. Kuthana ndi katangale. Kuba ndi matenda amene akudya Malawi koopsa. Mtsogoleri akuyenera kuteteza chuma Cha boma , kukhazikisa ma contract akafukufuku poyera, komanso kubweretsa chilango chokhwima kwa onse amene akuba ndalama za misonkho yathu.
Share this
Mfundo zina mu comment section ๐
10/07/2025
don't lose hope in us ...
we will bounce back with my team soon.
we love you guys.
๐น๐ท๐บ๐๏ธ๐ง๐ค๐ช๐ช๐ป๐ช๐ธ.
28/02/2025
โ๏ธ
28/02/2025
G๐โ๏ธ
๐
๐This politicians ๐๐...
Levels๐๏ธ
Don't be addicted to money. Work to learn. don't work for money. Work for knowledge.
Be strong
Be positive
Don't trust anyone focus on your goals...
Njeza Village
T/A Mabuka
Box 76
Mulanje
Malawi
Southern Africa ๐
...
12/02/2025
Don't drink and drive ๐ซ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Zomba