NVK
Mediam
09/01/2026
Bwalo la Supreme ku Blantyre lakana kumva pempho la mlembi wamkulu wa chipani cha MCP a Richard Chimwendo Banda, lofuna kuti asiye kusungidwa kundende podikilira mlandu oganiziradwa kufuna kupha munthu.
Oweruza Dorothy Nyakaunda wapereka chigamulochi ponena kuti pempholi lafulumira kufika ku bwalo la Supreme, chifukwa ati bwaloli limamva nkhani zimene zagamulidwa ku bwalo lalikulu.
Chigamulochi chadza mokomera mbali ya boma, imene inapempha bwalo, ati pozindikira kuti pempholi linalo ndi zolakwika.
Zateremu ndiye kuti a Chimwendo Banda akusungidwabe ku ndende podikilira siku la mlandu wawo, ndipo a Khwima Mchizi oimira a Banda, atsimikiza kuti a Chimwendo Banda akudwala.
Mchithunzimu a Khwima Mchizi
Wolemba Daniel Zimba
03/06/2025
Malinga - Nthawi Ndilibe [Official Video] Nthawi Ndilibe "I don't have time" a Morden dancehall song by Malinga empowering the youth to stay focused on their path and hustle, don't get distracted by...
Mongokumbusana
Tigers 2-2 Silver
27/04/2024
Nvk Feat. Ossy Kelly - Ndikazablowa(Official Music Video) Nyimbo
HALF TIME
CCAP 2-1 CATHOLIC
😂😂😂
NVK..nd nfana yekhayo amene
Akuyimba chamba cha
Dancehall kuchoka ku Be good alliance the best Dancehall crew
22/04/2022
NVK
FROM
BE GOOD ALLIANCE
THE BEST DANCECREW
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Zomba