Emmanuel Chikonso
Multimedia Journalist🎧📺📻
Current Affairs🗞
Politics 🎙
Sports 📡🏀⚽
Entertainment💽📸
18/07/2025
Passion
12/06/2025
Nzika imodzi yamdziko la UK Vishwashkumar Ramesh yapulumuka pangozi yandege yomwe yachitika chakummawaku mdziko la India ndipo inanyamula anthu 242.
Nzikayi inabadwira ku India koma yakhalitsa ku UK.
Ophunzira adzachipatala okwana 50 nawonso awagoneka kuchipatala kamba koti ndegeyi inakaomba Hostel yomwe amagona.
Matupi a Anthu omwe apezeka pakadalipano ndi 204. Airport komanso maulendo apandege pamabwalo andege a Gatwick ku London komanso Ahmedabad ku India aimitsidwa Kaye.
12/06/2025
BBC yati Pilot yemwe amayendetsa Ndege ya mtundu wa Boeing 737 ya Air India yomwe yagwa itangonyamuka kumene mdziko la India anali atatha Maola 8200 akuyendetsa ndege in short experience ya masiku pafupifupi 342 osatha Chaka, pomwe omuthandizira co pilot anali atatha maola 1100 yomwe ndipafupifupi masiku 46(miyezi iwirindi 2 weeks) akuyendetsa ndege.
Ndegeyi imachoka Ahmedabad kupita Ku London ndipo inanyamula anthu 242 pomwe inakagwera mkatikati mwatawuni mdziko la India. Pakadali nthambi zozimitsa moto komanso achipatala Ali pamalo angoziwo.
Mundegeyi munali nzika za India zokwana 169 , 53 za UK, 9 Portugal ndi m'modzi wa Canada citizens confirmed to be on board.
24/03/2025
Iwe Umati 🔥🔥Ndimaset avutawa 🎉🎊
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Nyapwe Tambuli, Fortun Canada, Dizzy Wally, Charles Thundu II, Kingdom Gondwe, Tiyamike Saad, Maliya Selemani
God is Great
06/04/2024
Super League Settings
19/10/2022
Let us be part of your Business Growth by having quality Designs and great Radio/Tv adverts from us
Just Wanna Try create a brand
and Market my Work🔥🔥
I am Mult-skilled. Ndimalowa paliponse.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Zomba