Blada
The Official page Of Blada.....Malawian Producer, Singer, Songwriter and Public Health Officer 🇲🇼 LifeStyle To Be On High
Yesterday was FiRE🔥
Oyimba ndi omwewa😃
20/04/2026
Yesterday was a BiG Day, Congratulations kwa ma artists omwe mwasankhidwa
wishing you all the best 🔥
17/04/2026
SPECIAL ANNOUNCEMENT ❗
Oyimba ochokela boma la Ntcheu mukudziwitsidwa kuti mutenge nyimbo zanu mupite nazo ku AWUZE pa boma pa Ntcheu nthawi ya 3pm ,awa ndi oyimba ozungulila pa ntcheu paboma,koma omwe muli kutali ndi paboma imbani pa number iyi 0881620638.
Izi zikuchitika pamene Company ya MASSA ikufuna izithandiza oyimba koma ochokela ku Ntcheu.
Tiyeni Tikayese Mwayi
16/04/2026
Good Morning From My Beautiful Queen 👑❤️
15/04/2026
UTHENGA ufike paliponse😀
Nyimbo ziyimbidwe mochuluka
#🗣️Blada!
14/04/2026
Lero ndabwelaso ndi chikwapu ichi, Chokwela mbambande
Iyi ndi
Nissan Xtrail 2013 model
M9R engine
Fuel type Diesel
Mileage 145000
4*4 mode
Imeneyi ikungofunika 20.5 Million basi NEGOTIABLE
Akutenga ndani iyi timvane
Contacts: 0987290020 calls / 0885140767 WhatsApp
13/04/2026
Dear Artists, Let's Work!
#🗣️Blada!
12/04/2026
Ine ndili BHO, ndili ndi LUSO!
#🗣️Blada!
09/04/2026
Ife ndi ANGONI AKU NTCHEU 😄
Tapezani yanutu pa mtengo wa bho, tangoona m'mene ndatchenelamo😄
Contact us : +265 998 32 73 55 (Calls or Whatsapp)
09/04/2026
Are you willing to Buy a Car??
Ndi CHAPS MOTORS anthu akugula ma galimoto abwinotu pa mtengo wa bho, Just IMAGINE galimoto mukuyionayi ndi
Subaru Impreza 2014 model
Mileage 73000km
Lane assist
Automatic transmission
Good sound system
Machine amwene, akupita pa 25 Million yokha komaso NEGOTIABLE, Mukaona Certified Producer akuyendela MAZDA DEMIO musazati sindinanene 😄
For More Information Contact us :
+265 997 18 29 10 (Calls or Whatsapp)
05/04/2026
New Song To Be OUT SOON!
Victoria - Ndakodwa
#🗣️Blada!
04/04/2026
Bro just surprised me with this😳, mfanayu ndiwaluso koopsya...I really appreciate the love ♥️🔥🔥
#🗣️Blada!
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Mphate
Ntcheu