Mphate CCAP

Mphate CCAP

Share

Spreading the Gospel of Our Lord Jesus Christ..

01/06/2026

Youth Comedy

01/06/2026

Kubwererako m'mbuyo pang'ono
12.04.2026

31/05/2026

31.05.2026


Chichewa Service

31/05/2026

31.05.2026

Nthawi ya kuwerenga Mau

2 Samuel 6:12-23 (Akwerra Nalo Likasalo Kuliika ku Yerusalemu).

Mateyu 18:5-7 (Wamkulu Mu Ufumu wa Kumwamba).

29/05/2026

PA Beteli sizinatiphonye....

Ladies & Gentlemen a very big hand for Wisdom Chimbe

🎓 Bachelor of science in Environmental Science with Credit.

Photos from Mphate CCAP's post 26/05/2026

26.05.2026


Tiyeni tiwerenge mwachidwi. 👇👇👇

25/05/2026

25.05.2026

📢📢📢ANNOUNCEMENT❗❗

Potengera mkumano omwe unalipo dzulo kwa onse omwe anali a Mphate Zone C, agwirizana kuti Zone yi igawidwe ndi maina a C komanso D.

Choncho tili ndi Mphate C imene ndi kuyambira pa Kasinje Turn Off, kudutsa M1 kufika pa Shop Ya Mtsitsa kutsetsereka mbali mwa mpanda wa Kings Foundation mpaka kwa Mr Dausi kukathera kwa Bambo Mjehani imeneyo ndiye Mphate C.

Kuchoka Kings Foundation mpaka ku Nkhande, Mbali inayi kukafika kwa chinyamula imeneyo ndiye Mphate D.

Inu muli mbali ti? Yenseyutu ndi Mphate CCAP, osasokoneza🤝🤝🤝

24/05/2026

Omwe alalikira lero ndi Bambo Maxwell Josinto akulu a mpingo opuma a Mphate C.

Ndipo atamaliza kulalikira uthenga omwe mutu wake akuti "Kodi Timakhulupilira kuti Tidzalangidwa?"
Inunso mukhoza kudziyankhira panokha, anafunsa izi poyerekeza nkhani ya "Nowa".

Utatha ulaliki Abusa a mpingo wu Rev. Ndalakwanji adalitsanso Uniform ya Mvano Choir pa Mpingowu.

24/05/2026

24May2026

Pakali pano tili mgawo la kuwerengedwa kwa Mau.

Ndipo kuwerenga koyamba ku kuchokera m'buku la Genesis 6:1-22_ "Kulowerera kwa mtundu wa anthu."

Kuwerenga kwa chiwiri Chipangano Chatsopano Mateyu 24:36-44_"Awachenjeza adikire."

24/05/2026

24May2026

📢📢📢 ANNOUNCEMENT!!!

MPHATE CCAP ZONE C, yagawidwa pawiri ndipo Ina ndi idzitchedwa C1 komanso Ina C2.

Tiyeni tonse amene tinali Mu zone yi lero tifike ku mlaga, tikadziwe Zone yomwe tili.

Ambuye akudalitseni.

Want your place of worship to be the top-listed Place Of Worship in Ntcheu?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Website

Address


Ntcheu