Ted The Reporter
Journalist, News, Audio & Video Editor, Director, Social commentator, Blogger etc...
11/12/2025
Ntchito za manja
20/07/2025
Follow Malawi Mouth-Piece mupeze ndalama
My favourite time โค๏ธ
๐ง Man: Bea Chifine chija bwanji pano:
๐ฉWife: Mmmmm bolani pano chayamba kuthako๐คญ๐คญ๐คญ
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Mary Woodworth, Kร sodo Dรญรฃmรฒรฑd Gift, Lily Chimtengo, Isaac Matola
25/01/2025
Us
Muli bwanji akazi nonse ofuna banja koma osalipeza kaamba ka mwano wanu .๐ฅบ๐ฅบ
0881120432,
0884442037
08999774053
0899904682
0990088737
Musankhapo number yoti museve kuti Ted The Reporter
Akanati chibwenzi chilichonse mwapanga chikatha azikupasani mbuzi ๐ bwenzi pano muli ndi mbuzi zingati?๐๐๐๐๐
Chibwenzi chikatha mutu umabalalika ,
mai ako kukufunsa kuti chavuta ndichani mwanawanga
umangoyankha umvekere
simungazimvese masten you are still young
๐๐๐๐๐๐
Mukapeza mpata muchite follow page ino.
Kodi chibwenzi chikatha zimatero ife chadzana tingotukwanizanabe mpaka pano ๐ซฃ๐ซฃ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Address
Mulanje