Victoria Kingstone..MP

Victoria Kingstone..MP

Share

The mission is to empower women and bring the girl child back to school, deliver tangible development

11/09/2025

Tikutero kumphunzitsa azigogo kuti asakaphonye pa Nkhokwe Yozaza ndi Chimanga.

11/09/2025

Ma umboni a mu 2014..Amen
Pa 16 September voterani Nkhokwe ya Chitukuko, yodalilika,yachifundo komanso yofikilika.

11/09/2025
11/09/2025

Ameen

09/09/2025

Moni kuchokera ku banja la Abiti Nkhokwe.

04/09/2025

Mlatho wa Mpeta watheka tsopano kuchokera ku mthumba la Mayi Nkhokwe amene aunkhonza ndi ndalama zawo. Uku kunali kuthokonza kwa a Mfumu a mpeta ponyadira chitukuko chimenechi.

11/08/2025

Voterani Nkhokwe yozaza ndi chitukuko.

11/08/2025

Zitukuko zimene Abiti Nkhokwe apanga...zigoli 70

11/08/2025

Zikomo kwambiri Thundu ward...nzoona osapanga mistake.

07/08/2025

Odi odi ku che Sanyila...Abiti Nkhokwe akwika kweleko

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Mangochi?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Mangochi