Awiri Beverages
We manufacture very tasty freezes in the following flavours:
1. Cola
2. Creme Soda
3. Raspberry
4. Orange
5. Pineapple
03/09/2026
Tithamange basi! Iphani makwacha ndi Super Cool Freezes. Freezes yekhayo wokoma zeni zeni 🔥🔥🔥
Belo imodzi K25,000 (100ml) komanso K2300 pa packet (50ml)
Tikupezeka ku Limbe mu Maa Hawa Arcade shop number 12 pansi komanso ku Blantyre Market
Ndipo ku Lilongwe tikupezeka pafupi ndi PEP yakuseli kwa Sana Supermarket yapa mzikiti
12/05/2026
Dzuwa ndiye lagungika! Zaodeni freezes wokoma wa Super Cool kuti mupeze phindu lochuluka.
Tipezeni ku Limbe pakapenga mu Building ya Maa Hawa Arcade shop number B12 kapena ku Blantyre Market.
Ndipo ku Lilongwe tili pafupi ndi PEP yakuseli kwa Sana yapa mzikiti.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Kamuzu Procession Road
Lilongwe
207201
Opening Hours
| 07:00 - 17:00 |
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Awiri Beverages posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.