DPP
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DPP, Political Party, Lilongwe area 46, Lilongwe.
VUTO MUNTHU AMAKANA KUZUZULIDWA, UKAMUZUZULA AMAFUNA NAYESO AKUZUZULE CHOLINGA MUFANANE. MUNTHU NDIOVUTA😑😑😑
27/03/2026
chonde chuma chathu chisakhale chozunzira anthu ena, chilichonse chamoyo chimanva kuwawa.
koditu ngongole munatengazo nzaife amalawi eni boma. choncho nduna ija poiphedula myumba ya malamulo ija amauza ife ngati mabwana awo (nzikazamalawi).
nde mukamati tika suma munsumira ndani? musumira wantchito wathu kapena ife mabwana? mumafuna bwana mwini ndalamazo asaziwe? taziwabe ndipo mubweza mufune musafune. muchita chosanza.
vuto andale akwathukuno akangoti akhala mbali yosusa nde amangosusa zilizose or mfundo zoti zithakutukula ziko lino amasusabe , chimene amafuna iwowo ndi kutenga mpandowo osati kuthandiza a Malawi.
kumabwalo anthu amirandu sikulibwino ayi ... mukutiuza kuti tizikhala mwa mantha chifukwa chanthu andalama, mulandu wamunthu okuba nkhuku two to 3 days umakhala watha wayamba Ku saver 2 yrs pomwe mulandu wa bwana wakatangale , kusakaza ndalama zaboma umakambidwa 5yrs kukhothi kenako muzanva kuti ndiosalakwa, koma ndalama zabomazo zinasakazidwadi anasakazayo sakuziwika...
muzaone ndende zathu zamalawi ndizozaza ndi amphawi anthu andalama sakhalisako. koma iwe ndine NDE ndikokaferako , kukalambira konko, ukachita mwayi umabwerako..
koma sibwino choncho
mmalawi munomo Ngati mulu anthu amene amapalamula milandu pafupi pafupi NDE ndianthu amdalamazawowa,
amapanga ma business a illegal, nkhaza ma industry mu, kuphyana malamulo apantchito, kusunga anthu mokakamiza, kubakumene, kugwiririra, kugwirisa ntchito mankhwala ozunguza ubongo, kuphyanya malamulo apansewu , ziphuphu ndikatangale, kuophyeza anthu ogwiranawo ntchito,
panopa zinafika poti bwana amaku challenger kuti ndalamazako za pension sulandira ukasume kulikonse ndilipira kumene ungakasume koma iwe ndalama yamga suiona or thawizina akakuona kuti ukufuna kupuma ntchito amangokupaka milandu ukakhale Ku police.
NDE timapempha akulu akulu abomanu chitanipo kanthumwachangu zinthu zikuonongeka izi.
timachita kusirira mmene mirandu ya anzathu maiko emawa imakambidwira mwachilungamo muja koma kuno eeeee katangale ndiziphuphu zamanga nthenje.
18/11/2025
SIDE NOTE: mukachosa moyo nzanu Ziwani kuti mwasala ndinu kuti muchosedwe moyo it's either anzanu kapena mwiniwake Mulungu kuti akuchoseni moyo. simungakhale a muyaya , muzafabe ... LIP
kuyambira January this coming term ma secondary school aboma fees ikuchosedwa siziperekedwa xool ndi yaulere pasapezeke mwana osapita ku xool.
CHONDE AKULU AKULU MBOMAMO NDALE ZITHEKAYE TIGWIRE NTCHITO, NGATI PALI ANTHU ENA OTI ANAPALAMULA MALAMULO AGWIRE NTCHITO TISATAYE NTHAWI NKULOZANA ZALA AMALAWI ANAVOTA NDICHOLINGA, TISAWAKHUMUDWISESO , MMIZIMU MULI MAKOLO ATHU AKUVUTIKA TIYENI TIWAFEWESERE ZINTHUZI AZITHA KUZIPEZERA PAOKHA MOPHWEKA.
OSADANDAULA AMALIWI POMANO ZINTHU ZIYAMBASO KUYENDA TISAFOOKE TILIMBIKIREBE NGATI MMENE TIMAPANGIRA MUJA, OSATI ZIJA AMAKAMBA ANDALE ENA KUMATI, MMALAWI NDIWAULESI. TIKHALE AULESI CHIFUKWA ZANU ZAYENDA, AMALAWI MDI ANTHU OLIMBIKIRA AMANGOSOWEKERA ULAMULIRO WABWINO..
Boma lomwe lachokali likupanga ma plan oti azipeka nkhani zaboza ndicholinga choti ayipise Boma limene liripoli , Koma ndi umbuli, DPP inkatsusa nkhani zoona osati zongopeka...apusanazo izi I thing kukuoneka Kuti kulibeko anthu anzelu zawo.. kwazaza buli zokhazokha...
akuluakulu tiyeni tirimbikise ntchito Zama company ndi ma industries nziko muno, ndika phone komwe Ka keypad tizichita kukagula ku China zoona Pali nzeru , screwdriver, Boart and nurts, usb cables, memory cards, speakers, earphones.......
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe