Precious Electronics
Want to buy a Phone? WhatsApp 0891562857. Precious Electronics sells electronics products from phones and computers to rice cookers and refrigerators.
02/06/2026
Monga kunalonjezedwera. Anthu 7 awa anapanga tag anzawo mwamkokomo ndipo awina ya bundle.
DM your tnm numbers ONLY pa FB.
02/06/2026
Zatengenkoni imodzi apa
WhatsApp: 0891562857
02/06/2026
Phone ya madolo iyi 🔥
💬0891562857
02/06/2026
Admin watopa nde azingoponya ma verse basi
01/06/2026
0891562857
THE BEST DEAL 🔥
Rom 6gb ✅
Space 128gb ✅
Cash ✅
Layby ✅
Brand new ✅
💰400k ✅
WhatsApp: 0891562857
Redmi note12 pro+ 5G, 625k,
WhatsApp 0891562857
Xiaomi 11, 256gb, 💰835k
WhatsApp 0891562857
01/06/2026
Ife sitili ngati chibwenzi chanu distance singatipange separate. A ku Mzuzu phone tikubweretserani. Kulikonseko timafika; osaopa.
Amene apange tag anthu ochulula kwambiri mu comment section iyi awina ya bundle.
Zoyika screenshot ayi. Mupange tag mu comment.
Tigawa ya bundle kwa anthu 7. Tiye nazoni.
01/06/2026
Tinfunsa kuti tipange chani kuti tigawe bundle kwa anthu 8. This suggestion ndiyashapu, so we will do that in the next post.
Guires ponyani number yanu ya Tnm ku inbox tikupatseni ya bundle for the great suggestion.
KONZEKERANI NEXT POST KULI MAYELE!
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Address
Guoji Shopping Mall Area 49, Shop C13B
Lilongwe