Enock
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Enock, Grocers, Lilongwe central market, Lilongwe.
03/06/2023
Malawi ayenerakukhala osamala ndi malamulo akujawa monga malamulo omwe amerika akukakamiza maiko amu Africa pamaukwati Amina kapena akazi okhaokha chifukwa chauphawi tikupepha azitsongoleli anthu amipingo ngwilizanani ndikungwilana manja kuti muyesese kukana zamchitidwe umenewu kuphatikiza andale nonse chinthu ichi chidzatibweretsera mkwiyo was mulungu kutsongoloku choncho tikhale osamala.
Koma ma demo amawa tonse kulira kwanthu nkumodzi tikakapereka kalata koperekako basi tizikabwerera osati Ena omwe amapezerapo mpata omaba ndikuphwanya zinthu zaanzanu omweso ndi olira ngati Ife yomwe sibwino akakupezani akumangani ndinu mbava sizamademo zimenezo, tiyeni tilemekeze ufulu wanzanthu chonde tonse ndiolira ndinthu Viva malawi.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Lilongwe Central Market
Lilongwe