S third
F . E. A .R 😄😄
just smile
It hurts 🥹🥹🥹
I hope 🤞 that you know
06/10/2025
President Peter Mutharika wasankha nduna zake zitatu zoyambilira komanso ma udindo ena akuluakulu m'boma.
Ena mwa ma udindowa ndi monga a Enoch Chihana kukhala wachiwiri kwa wachiwiri wawo (Second Vice President), Dr. Justin Saidi kukhala mlembi wamkulu waboma, ndipo wachiwiri wawo ndi a Stuart Ligomeka.
Pomwe a Kiswell Dakamau awasankha kukhala mkulu owona za nyumba zaboma.
President-yu wasankhanso a Richard Luhanga ngati mkulu wa apolisi mdziko lino. Achiwiri awo ndi a Stain Chaima ndi a Noel Kaira, pomwe a Lieutenant General George Jafu ndi mkulu owona za nthambi ya asalikali mdziko lino ya MDF.
Nduna zomwe azisankha pakadali pano ndi a Alfred Gangata, George Chaponda komanso a Joseph Mwanamvekha.
(by Innocent Kumchedwa -Lilongwe:10/05/25)
let them talk
Put in
God first 🙏🙏🙏🙏♥️♥️
Love 💕💕💕💕
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Pre Chee, Monticalvo Roldan Vlog, Remina Bonggo Avelino, Edgardo Santillan, Seun Piezu
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe