Malawi Daily

Malawi Daily

Share

This Creative Centre is here to educate and inform guardians on different aspects concerning childre

Photos from Malawi Daily's post 28/12/2024

INE NDI NDANI....? ❤️

28/12/2024

🚨Heartbreak of the year...💔

Basitu woyimba wamkazi, Hezel Mak, angomusiyira mwana kenako mamuna wawuyatsa ulendo, banja latha.

Pepa, Hezel. Heaven is the goal!

Apa walowa gulu lama single mums lachina Miracle Chinga, Tamia Ja…

28/12/2024

Mpangeni tag mwini nkhaniyi

23/12/2024

Madeya ayambile panja mpaka nyumba mwanumo Nkhuku ikalowa sekani chitseko,,,mapezedwe a Mpunga tiphunzitsana mawa... Xmas🎅

21/12/2024

Oimbila mpira wamiyendo okwana khumi asanu ndi mmodzi avomelezedwa ngati a FIFA a dziko lino.

Pa oyimbilawa pali Godfrey Nkhakananga, Easter Zimba, Mayamiko Kanjere ndi David Chinoko.

Kumbali ya othandizira ndi Bernadettar Kwimbira, Clemence Kanduku, Pondamali Tembo, Happiness Mbandambanda, Evance Msonda, Lameck Phiri, Samuel Fudzulani, Mphatso Matete ndi Sibusiso Sibande.

Koma kumbali ya oimbila omwe akhoza kumaunika nawo pa kanema (VAR) palibe yemwe watengedwa mdziko muno kamba koti Nkhakananga, Gumbo ndi Tembo onse akanika.

Rose Zimba wakanika kukhala nawo pamndandanda wa FIFA.

Zabwino zonse

21/12/2024

Congratulations to Mighty Mukuru Wanderers FC for being crowned the 2024 Castel Challenge Cup Champions.

Photos from Malawi Daily's post 21/12/2024

Bad day for the Cities

20/12/2024

Mozambique ndi chifukwa chimene chimachititsa kuti Tanzania izifuna mbali ina ya Nyanja ya Malawi. Tikuganiza izi chifukwa mbali ina ya nyanjayi ndi ya dziko la Mozambique. Chifukwa choti tinatema kumupatsa neba (Mozambique) naye neba winayu (Tanzania) amafuna titamutemere.

Kumbukirani kuti ngakhale boma la Likoma ndi limodzi mwa maboma a ku Malawi koma bomali limapezeka mbali ya nyanja yomwe ili m'manja mwa Mozambique. Ichi ndi chifukwa chake mzere osonyeza malire a dziko la Malawi ndi Mozambique (international boundary line) umaoneka kuti unadutsa m'nyanja ya Malawi.

18/12/2024

Just because he dated u for 4 good years doesn't means he will marry u.
My uncle study medicine for 8 years and he is a DJ now.

14/12/2024

Entertainers of the Year— music category winners

Male Secular Artist of the Year
Driemo

Female Secular Artist of the Year
Emmie Deebo

Male Gospel Artist of the Year
Steve Wazisomo Muliya

Female Gospel Artist of the Year
Miracle Chinga

Secular Song of the Year
Kutali by Fadda Motti

13/12/2024

Mutawapeza mungawatani

13/12/2024

Jetu akupuma kuyimba chaka chamawa

Oyimba wachikulire, Jetu adzasiya zoyimbayimbazi chaka chamawa. Dyokhwe, m'modzi mwa adzukulu ake a Jetu, watsimikizira za nkhaniyi.

Iye wanenetsa kuti kaya aMalawi mufune kaya musafune koma Jetu akupumila zoyimbazi chaka cha 2025. Mkufotokoza kwake, wati Agogo akewa akudzapuma kuyimba chifukwa akalamba kwambiri.

Pakadali pano, Jetu yemwe ali ndi zaka 73, watulutsapo nyimbo zingapo zimene zikusangalatsa anthu monga, Wakalamba Wafuna, Chakwaza, Simunatchene imene anayimba ndi m'dzukulu wakeyu ndi zina zambiri. Jetu watulutsaso nyimbo ina yotchedwa 'Waimanya' masiku anayi apitawa imene anthu akuikondaso kwambiri.

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Lilongwe