LIDDECHi74

LIDDECHi74

Share

LIDDECHi74(Ghetto Warrior)
Blantyre,Malawi
Hip-hop artist (rapper)

YoungBlesser as well😎 ghetto rapper

12/02/2026

LIDDECHi74 - Rhymes@25_ Now Out🔥
Official music video 📹 ❤
https://youtu.be/eYvDkq5SUpY?si=_8FQGCvxKSPZQbA1

18/10/2025

Amandiwaza akamati ndika munthu kabho/ndimamvetsa akapusha nkhani yovaya temple/kumupatsa chuma sayambitsa CHOIR, ndukuuzani life yake aMASINTHAtu/

"Mzika part 2" coming very soon🧖🏿‍♂️

17/09/2025

Bwana Kalawe mukanakhala kuti ndinudi ozindikira izizi mukanayankhula earlier osati poti Kabambe akutsalira, inuyo ndongofuna attention kuti muzioneka anzeru- otherwise ndinu abulutuso.

SIX REASONS WHY KABAMBE FAILED TO FIT IN CHILIMA'S SHOES 👟

1 Messaging

Chilima, naye ngati Kabambe, anali wa Economics. Koma akamapeleka uthenga amayakhula zoti muthu wakumudzi amve.

Kabambe mbali inayi amaveka ngati lecturer wa Economics, amachulutsa ma jargons oti munthu wakumudzi alibe nawo ntchito.

Chitsanzo:
Kabambe - panopa import cover yathu ili less than one month ife tizayikweza kufika pa 3 months kuti feteleza azipezeka anthu akolole akhale ndi chakudya.

Chilima - muzizadya katatu pa tsiku.

2 Charisma

Chilima anali wachikoka. Amati akayakhula dziko limagwedera.

Kabambe amati akamamaliza kuyakhula anthu amakhala ayiwala kale zomwe wanena. Nothing to remember. Five years later timakambilanabe za speech ya tizafera mbendera. Ndi speech iti ya DK yomwe tingakambilane lero.

3 Innovation

Chilima amabwera ndi zithu zachilendo. Ma whistle stop ake ankawatchula kuti imbizo. Anayambitsa ma live coverage amisokhano ndi zina zambiri. Kabambe chanyuwani anapanga campaign yonse mkupita pachi giledala kuma nominations.

4 Symbolism

Chilima ankadziwa kuti anthu amakumbukila ma symbols. Nde amatha kungobwera ndi legeni ati yophera pumbwa. Kubwera ndi mthumba la 50 kg nkuli header. Kumenya ma push ups.

DK amangobwera ngati akuzatiphuzitsa Economics 101. Chomwe chimatsalila ndi choko ndi duster.

5 Reality over ego

Chilima ali vice president analolera kukhalaso vice chifukwa amadziwa kuti kulibwino kukhala vice wa ngwilizano than kuima yekha mkuluza. Decision yake sinali emotional .

Kabambe amatsogoza mtima. Sangamtero. Nde kupanga zithu zongokula mtima koma zoti amadziwa kuti sizitheka.

6 Chilima ankawadziwa anthu ake. Kabambe samawadziwa. Akanakhala amawadziwa pa Vice akanaika Fredo chifukwa Fredo anali ndikuthekera komweretsa ma number koma Mtumbuka olo u MP kwawo waluza ndi landslide. He can't appeal to his own.

Hard lucky DK. Keep learning, tsiku lina zizayenda.

06/09/2025

We're about to drop a banger! 🎶 Sones and I collaborated on a fire track– let the lyrics speak🔥 "Ndakulira Mu Ghetto" official music video coming soon! 🚀

Hip-hop ndiyatonse✊🏾

20/07/2025

I think this is the perfect time to advise these kids about how people fake things on social media. Anyway, I'll be releasing "Mr Little Boy" in the coming weeks. Enjoy the verse for now 💪

22/04/2025

Attention seeker Dr Namadingo🚮

18/04/2025

Happy Easter! Wishing you joy and blessings🙏💪

PANO LIDDECH74 VISUALS BY MANCA 11/04/2025

Munena bwanji kuti afana amatha/angotsatira energy ndi zero bola fanta/mafana oti ali pompaja, sasuntha, mindset ndiyongaza, iwe sukumva/

PANO LIDDECH74 VISUALS BY MANCA 3A ENTERTAINMENT

02/04/2025

Tilipo! Chilichonse tikupanga aseh/
Mafana amangokamba timapanga aseh/
Tsiku lomwe anayakitsa'lo ndi liti aseh/
Ndimauluka pa beat ndine mfiti aseh/

Kulikonse ndimapereka chi busy/
Mafana onsewa sangatinyumwise/
Tipatse beat tikhaulitse/
Timayika zima bars ngati prison/

Limbani olo mutabwera 2by2/
Kutchaya kugwetsa crew by crew/
Mafana mwachepa tavayani ku xu/
Ayimbe zongaza amveke ku gulu/

Tell Ace Jizzy beat ya Dodi Dodi kunonso ndaidoda💪

17/03/2025

LIDDECHi74
Hiphop/rap artist🤜

13/03/2025

EXCITING NEWS!

The official music video for "Pano" is finally here, Watch now and let me know what you think!
https://youtu.be/BmyKZ9Z82wk?si=g_AcSmzAX6G14k_x

LIDDECHi74 Alice Namathanga

04/03/2025

No more setbacks this year🤲
LIDDECHi74

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Zingwangwa (blacksea Street)
Blantyre