EngAllan
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from EngAllan, Digital creator, kanjedza Blantyre, Blantyre.
11/06/2026
Support Mexico 🇲🇽 to avoid being accused of taking their jobs.
11/06/2026
Big shout out to my newest top fans! 💎 Kondwani Tsitsi, Mau T Maunde, Abiti Maunde, Mphatso Mwachumu
fans
09/06/2026
AYUBA JAMES, MP WA MCP AKUTI MWEZI WA JUNE CHIFUNGA CHAMAVUTA,
WALEMBA IZI
Dzulo ndege yomwe tinakwera kubwera ku Blantyre inalephera kutera itayesera koyamba pa bwalo la Chileka chifukwa Pilot amalephera kuona njira kamba ka changululu (fog).
Pilot anaikwezanso ndege ndikukazungulira kaye kawiri, kutulukira mbali ya kumadzulo, kwinaku akulengeza, kuwaunza anthu kuti asataye mtima, iyeyo akusaka poterera chifukwa utsi wa mmitambo wamutsekera njira. Koma ambiri tinadzidzimuka titatulukira mmbali mwenimweni mwa Phiri lomwe lili kumadzulo kwa bwalo-li, kupangitsa ambiri kufunsa ngati pilot amaliona phiri-li.
Lero ndimayenera kubwerera ku Lilongwe masana cha mma past 3. Koma nditaimba phone ku airport kumupempha munthu kuti andilowetsere dzina langa mu maina a anthu omwe akukwera ndege ndi kundipatsiratu mpando ndege isanafike (check-in) chifukwa ndifika mochedwa, ndinaunzidwa kuti ndege lero inyamuka usiku kupita ku Lilongwe, chomcho mdisavutike ndi kufika 2 koloko kapena 2:30 ngati nthawi zonse.
Nditafunsa chifukwa chake, ndinaunzidwa kuti ndege dzulo ikuchokera ku Kenya inalephera kutera pa bwalo la Kamuzu ku Lilongwe chifukwa cha changululu (fog) ndipo ngakhale anayesera kambirimbiri, oyendetsa ndege sanakwanitse kuona poteretsa ndege-yi ndipo mmalo mwake inapitilira ku Zimbabwe komwe inakatera ku bwalo la Harare komwe inagona. Izi zinapangitsa kuti lero ndege ichoke kaye ku Harare kubwera ku Lilongwe, komwe inavutikiranso kutera, isananyamuke kupitanso ku South Africa, komwe yapita masana mmalo mwa mmawa monga nthawi zonse.
Mmawa wa lero, ndege-yi inachedwa kunyamuka ku Harare chifukwa inaunzidwa kuti ikafika msanga idzalepheranso kutera chifukwa changululu chinali chambiri pa bwalo la Kamuzu ku Lilongwe.
Pakadali pano, tikanali pa Chileka kudikira ndege-yi kuchokera ku Sasafilika kuti tidzibwerera ku Lilongwe.
Dzulo panali pa 7 June, 2026 ndipo pa bwalo la Kamuzu palibe mapiri aliwonse omwe angapangitse kuti changululu chichuluke kwambiri. Changululu chimakula kwambiri mmalo a mapiri, kuchitira inu anzathu owuma mitu omwe simumaimvetsetsa Geography ndi Sayansi koma ndinu akatswiri pa nkhani za kayendetsedwe ka ndege.
08/06/2026
Tchamani
05/06/2026
Chinese, Japanese, Taiwanese and Koreans don't speak or write good English but are prospering through industrialization and trade. In Africa our biggest conversations are ; who speaks better English which is not even an African language, which country have ladies with the biggest nyash, which country practice religion the most. So stupid things we can be discussing in this Africa .
04/06/2026
🌍🏆 From the 700 players who went to the World Cup in 2006, only four will be there in 2026. Legends 🇵🇹🇲🇽🇭🇷🇦🇷
Once you see a bricklayer drinking in the afternoon just know that one bag of cement is missing.
Kids in the future will be hearing stories like, I left your father because he wasn't picking up my video calls.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Kanjedza Blantyre
Blantyre