Finaltouch
finaltouch IT & Electronics is Malawi's best repair shop for computers and other electronic gadgets.
06/06/2026
Khasu silimakhala lokongola inu, umakhala okongola ndi mpeni odulira cake et? kkkkk apapatu ndipomwe pamachitikira matsenga athu , ka battery akaka kamapanga zamatama customer anakagula ndikungosiya kwa 2moths osakagwiritsa ntchito ndiye kanaloka.
Eya battery limakhala ndi firmware ndipo firmware imeneyi imapanga detect changes in voltages and current mukamachaja or mukamagwirita ntchito, Ngati mwangosiya battery lanu osatchaja kwa nthawi yayitali voltage imatsika mpaka below the optimal voltage, zikatere firmware ija imaloka kuti ma cells asafoile.
So ngati izi zinakuchitikirani dziwani kuti battery la PC yanu ndilotheka kukhala ndi moyo.
NOTE : Ma battery ena amakanika kukhoza chifukwa IC kapena firmware yake siili supported ndi Battery Analyser.
Nthawi zina zimafunika nthawi yaitali kuti battery lipangidwe calibrate siza 30 minutes yatheka.
05/06/2026
Zomafunsana kuti aise sand paper bwanji tipangire clean chootchelera kapena kumazitama kuti muli ndi ma jeans abho mumangokhukhuza soldering iron pa trouser nzachikale ndipo ngati mukupangabe muzazindikira kuti mumachedwa mukadzangoyesa ka Soldering Iron Tip Cleaner akaka.
Ubwino wake momveka bwino ndi uwu;
Soldering iron tip imakhala ya clean heavy,
Soldering iron tip imakhala yolimba chifukwa temperature simapidwa affect popanga clean.
Soldering iron siimachepa size
iiii basi ndatopa ndikulemba kwinako muzipanga comment nokha mukagula.
04/06/2026
Or muwafunse anzanuwo ifetu tilibe nsanje, Timakonda kuti aliyese azikhala osangalala makamaka masomphenya ake okhala Technician wa bho akwaniritsidwe thats why sitimabisa info.
Inuyo ngati mulibe BIOS Programmer koma mumakonza ma PC nthawi ija ndi ino kuti mupeze yanu pa price ya bho pati.
Inuyo kugula akaka simunabetse coz simungaflashe ma computer 5 yake isanabweze. Izizi ndikunena coz i love you.
04/06/2026
Ndiye pali ka staff akaka ngati mulibe tip yomasulira screw ya device yanuyo ndiye kuti imeneyi si electronics koma mechanical device.
Kakafunika bwerani tizasinthane ndi ndalama inu muzatrape mishan imeneyi, inuyo muzioneka uyaza pa mpanje pano.
04/06/2026
Zomagogoda waya kapena kumasulira mpeni ma device anu si deal.
Tayesaniko ti ma set ta sharp iti.
03/06/2026
Lero pa table pathu panali chakudya chimenechi ndipo sitinamalize tasunga mkute mawa tili nawe nawe Intel Gaming motherboard wamvwa.
02/06/2026
Get professional IT support without leaving your home or office.
✅ Fast Assistance
✅ Save Time & Transport Costs
✅ Quick Problem Detection
✅ Affordable Expert Support
Computers malfunctioning? Software Errors? Network Problems?
Let us diagnose your device remotely.
Finaltouch IT & Electronics
+265 981 553 576
Professional Remote Support from as low as K20,000/hr
Terms & Conditions Apply.
02/06/2026
This how we started our day on Monday. Happy new Month.
Mafana awawa anali ready for delivery same day of arival. The other one was not displaying and ka dell ko sikamapanga detect ma SSD .
Both pc have have been successfully fixed, tested and delivered to our valued clients.
Inu successful repairs depend on many factors, and not every repair can be completed within a single day. Some issues take only minutes to resolve, while others require more time for proper diagnosis and repair. Please note that we prioritize repairs booked through appointments.
Hallo. Mulipo? eya ife tilipo tinasowanatu, ma admin anali busy kwambiri kufixa ndi kusova ma queries, Watch out this space we have some important updates coz eeee week ino kuli ambiri.
19/05/2026
Ife zaubwino wa ma keyboard awawa tinatopa ndikulongosola kalekale...................
Sitinalandilepo claim ngakhale imodzi, ma customer amangotimwetulira tikawagulitsa ma keyboard amenewa.
Kopezeka ife mu limbe ndipo ma nambala athu ndi 0981 553 576 /0884 553 576
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Livingstone Avenue Limbe
Blantyre
312229
Opening Hours
| Monday | 08:30 - 17:00 |
| Tuesday | 08:30 - 17:00 |
| Wednesday | 08:30 - 17:00 |
| Thursday | 08:30 - 17:00 |
| Friday | 08:00 - 17:00 |
| Saturday | 09:00 - 14:00 |