Prophet Y Simujah
FAITH IS NOT JUST BELIEVING THERE IS GOD,WE HAVE TO OBEY HIS WORDS.
06/01/2026
➖When you hear of wars and rumours of wars know that the end is near {Marko 13:7}.
➖Christ is coming sooner than we think.🙌
SUNGANI MAU AWA
➖Kulephera kwanu kwa lero ndicho chipambano chanu cha mawa ngati simufoka mtima.
➖Mwapemphera kwambiri koma sizikuthekabe,ziwani kuti Mulungu akukonza chithu chachikulu pa moyo wanu,nde musafoke.🙌
NDI ANTHU OCHEPA KWAMBIRI OMWE AMAYAMBA CHI KRISTU NDIKUCHIMALIZA MOYENERA.
➖Ngati munthu sakukwanisa kumvera bwino-bwino Mulungu,amagwa,apo ayi amalowedwa mizimu ya chisocheretso.
➖Timayenera tikhale anthu omvera kwambiri ngakhale mu zithu zomwe sizikutipasa tanthauzo.🙌
04/10/2025
➖Mukazaona anthu ena akuyakhula zonyoza ena pa social media osazanyoza nawo Ngakhale onyozedwawo atalakwisadi.
➖Satan amatha kumpangisa munthu choipa ndi cholinga choti ena anyoze ndipo akanyoza atembereredwe pamodzi ndi ochita choipayo.
➖Kunyoza ena kumabwelesa matsoka patsogolo.🖐️
PARTNER OYENELA
🌹Munthu Yemwe angakukonde kamba ka maonekedwe ako okha kapena kamba ka zithu zomwe uli nazo,sangakwanitse kukukonda moyenelera m'mene zimafunikila.
🌹Mkazi/Mamuna wabwno amachokela kwa Mulungu. chako.
KHALIDWE NDILOFUNIKA KWAMBIRI
🌹Ena adati Khalidwe ndi chuma,mau amenewa ndi anzeru kwambiri chifukwa ndaona anthu ambiri akulephera kupeza znthu zabwno kamba kosowa Khalidwe.
🌹Asikana ambiri akulephera kupeza ma banja abwno chifukwa chosowa Khalidwe,ena mwano,ena Kuzikuza,ena chipongwe ndipo ena chifukwa Cha moyo wawo wa social.🙌
04/05/2025
MONGOZIWISANA
Betting,Lotto,Pool and all forms of Gambling is a Sin,
Mwana wa Mulungu sakuyenela kuchita nawo zimenezi.🙌
14/04/2025
➡️ Kupusa kwa munthu kwagona mukusaziwa,tonse tidakaziwa zomwe zili ku tsogolo,bwezi tikusatila Yesu ndi Mtima wathu wonse 🙌.
KULIKHIDWA KWA MTENGO WAUTALI KU MALAWI 🇲🇼💔
➖Zithu Zina zooneka ngati zosakoma zikamachitika ku Dziko anthu ambiri amangoganiza kuti akuchita ndi satan.
➖Ayi ndithu,Zina zimakhala kuti akuchita ndi Mulungu kuti anthu amphunzilepo kathu {Alape}.
➖Mtengowu mu Dziko lauzimu ndimaona kuti akuulikha ndi Mulungu mwini osati Satan,ndpo Mtengowu wakhala ukupasidwa ma WARNING ochuluka koma udaumisa khosi kamba ka mapangano adziko lapansi omwe udalowa.
⚠️Mtengowu ukalikhidwa anthu ambiri ku Dziko azayakhula zosiyana-siyana zonyoza anthu ena koma omwe mungawelenge post yi musazayakhule nawo chifukwa akupanga izi ndi Mulungu mwini.
,zimangofunika kumukhulupirira Basi.
Odali Ali iwo amene akhulupirira ngakhale sanaone chifukwa zonse zomwe azikhulupirira zizachitika ndithu.🖐️
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the place of worship
Telephone
Address
Machinjiri Khama
Blantyre