Major Pest Control
MAJOR CLEANING AND PEST CONTROL
07/05/2026
This term,We have fumigated 48 Schools so far through the Kuthana ndi Nsikidzi project.
Our aim is to help Students maintain good hygiene and prevent Bedbug infestation in Schools.
For Fumigation Service 0990471156
Tchulani Boarding School yomwe kumavuta Nsikidzi.tione kuti Tipange nayo bwanji
31/03/2026
Wina pamudzi pano wina tizamuzizimusa oneday ka iPhone 11 kokha.tachokesana kutali Ndipo mwatipasa supportš
Thank you for the support. MD of Major Pest Control came to support us š„
18/01/2026
Kwa Top Fan kumumvesa kukoma š¤£
10/01/2026
Akuti Ali ndi company ya Fumigation Ndiye ku Nyumba kwao Kuli Nsikidzi Koma akapanga Fumigate sizikufaš¤£š¤£ Ndiye atiimbira phone kuti tizawathandize tiwaphere Nsikidzi
Nanu imbani kuti tikuthandizeni.
0990471156
Ndi ifeyo kupha ma Pest Zimathekatu.
03/11/2025
Tipaseni Malo Olo Katundu wanu kuti timuyangāanire, Ife a Major Security Services tili ndi ma Guard a Discipline komaso oziwa kugwira bwino ntchito 0990471156.
07/10/2025
Kampani yopopela msikidzi, Major Pest Control ikufunila Zabwino Zonse Kwa HE Prof. Arthur Peter Mutharika ndi aVice awo, Justice Dr Jane Ansah SC. JA ( Retired ) pamene akuwalumbilitsa lero ngati atsogoleri adziko.
08/09/2025
Tili ndi Nkhuku zogulisa here in Blantyre, Nkhuku imodzi ikugulisidwa pa K20,000
0990471156
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Blantyre
123