MBH
Music Promotion, Adverts, Arts, Entertainment, Celebrity Gossip kuchimake

Malawian musician Tay Grin has won the Tourism and Culture Promotion Award at the Diaspora Economic Forum for promoting Malawi's cultural heritage through music and international representation. Mmmmm awa m awards ndiye zinawayanja..

Happy birthday TC11 Chawinga.
Inuyo ndi pangolin MAMA.

NAZOMBE FAMILY.
Ngati mmalitsatila banjali kunachoka ana okonda dziko lawo okhaokha. Munyengo ino tili ndi uyu Devlin Nazombe AKA Mmisili opanda zida. Amabebetsa pa wailes,kuitanila malonda,Mc, amalakatula ndi wa usilu ameneyu anaphangila zonse. ππ Big up asee... get your flowers πΊπΉπ₯
ATHU MULI KU JONI EISHHH MUKULOWETSATU MIFUTI DZIKO MUNO. DZIKO LAYAMBA KUOPSANO ILI. MMMMM.

Koditu mkazi uja yense amaoneka chonchi. Social media.

Malehu aku Zimbabwe tsopano ayamba kumalandila Nyemba ndi chimangangati malipo mukawathila batile.
I think malawi we are still thinking about it tikhala kumapeto........

Hie MBH
Eishhh zandivuta amwene, ine masiku apitawa ndadya mkazi winawake ndiye ndimati ndikazulamuja amandiuza kuti ndisope b4 I put In again, koma ndikamasopa muja ndi amalilira kwambiri akuti akunvabwino. Lero after two weeks onani kukamwa kwangaku ? Ndichani zimenezi? Kodi ndipangebwanji? Madam anga ndiye anyanyala apita kwa kukhala kwa Bra yawo ku Chilobwe. Eishhh akaziwa ali ndi matenda koma samaonekera fast ngati amunafe!!. Help me please π

Mwina mkaziyu adakali single mpaka lero. Chifukwa 2020 15 October ndikale ndithu. Mfumu yathu. TAY GRIN.

Ali ndi mwayi otuluka kupolisi kuja koma pokhapokha atapeleka mk 50,000 koma akalephera akakhala kundende kwa miyezi 12 basi.
Paja Mayiyu yemwe amagulitsa mzimbe, anayimbira foni amuna ake kuti anthu ena amuba ndipo akufuna 500 000 kwacha kuti amusiye. Mayiyu anatinso, anthuwo amuba pamodzi ndi anthu ena 20, ndipo 14 aphedwa.
Nthawi ya mlandu, mayiyu anawuvomera mlanduwu, zomwe zinachititsa Senior Resident Magistrate Bracious Kondowe kulamula kuti alipire 50 000 kwacha kuti atuluke. Amene muli ku Lilongwe chitanipo kathu...

Mkazi ameneyu Morton Baghaya sakugona naye tulo...

Seven men have been convicted and sentenced to 21 years imprisonment with hard labor for robbery. They broke into a shop at Gravity Mall in Lilongwe, stealing K20 million cash and other items. Police recovered a pistol and toy gun used in the crime.
Tipatssane moni pano kuti mwadzuka bwanji?
Ife tithokozenso Mulungu kuti tilibwinonso ndithu Kaya inu?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the establishment
Telephone
Website
Address
18844 Lenchman Street Bloekombos Kraaifontein
Cape Town
0684323707