Da Kim
Content creator/intertainer & comedian
For promo [email protected]
Let us promote your music and business π€
06/16/2026
Ali mwai ayithesa msanga game yi nakavala kit kuti ndingowachinyira ndine a Senegal π
06/16/2026
Inde onse ndiachikuda koma mwakwera yitiπ€π€A Senegal say helloπ§β½π
Phindu la iwe ndi chani ? π₯± Keep resting in peace izek and JakoboποΈ
06/11/2026
Xenophobia πΏπ¦ VS π²π½ Mexico
Team Mexicoπ₯π₯π§What about you???
Singavaye Out ngati Kicks yada π kodi ma slime tandipaseni dzina lachi Slime apa iya π
06/08/2026
Singavaye Out ngati Kicks yada π₯± koma kicks yanga yikuoneka kumeneko ma Don dada Top shatta ndi Abale ?
Mzuzu pa 27 june Chisanga complex mudziwaso, tikumane ku show iyi you never know ndizakhala MC ku show yimeneyi paja sindipanganika tu π₯π₯
Team Ca$ino, team Em EL and Tkas mwakhala pati ma Top shatta ? nde chikazati singaduke ngati Anemwe tili bino bino asaaa kukakoma uku π₯π₯
see you all there
06/05/2026
Kizito Waxy Kay zikomo popanga Artwork ya nyimboyi, ndipo artwork ndiyomweyi yangosala nyimbo yo yituluke basi π₯
Tamukodoleni mzanu okonda mabodza yo amve nawo a new one π₯±
Kizito Waxy Kay kupangidwa surprise ndi Girlfriend wake, Bola tisamve mawa Mamie Mary Kapenga awotcha sapato yo ππ
Ndi angati amene nyimbo izi zikutibalalisa ? π₯Ή
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Federal Way, WA