Prove cee
Jus vien mw
29/04/2026
akupeleka mon kwa nonse amalawi ak*t mudikile akakula azkuyendelan nonse komaso ali ndi nyimbo yomwe ituluke posachedwapa tereza tex pangan follow k*t muzathe kuvela nawo luso lamwanayi
29/04/2026
potengera k*ti iye ndi silikali anasakha k*ti chilichose chomwe chili nyumba mwake chizikhala chofanana ndi ntchito yake nakha munthu okuba amasakha chani choti chizifanana ndi ntchito yakeπππ€£π€£
29/04/2026
zithu zikasitha tikuuzani
29/04/2026
chikondi chizionekaso pamavuto kell kay sananyozer koma kupita kukamuyang'anila zeze kuchipatala munyengo zonse zeze musamusiye yekha yehova mukhale naye paka kuchilaππππ
21/08/2025
Kuli ndani uko ehe kulindan uko DPP
Vote yanga sikundipindilira π²πΌπππ
03/10/2024
Jay jay cee anakondwa kwambiri olo mene anagwiliramo ayi sitinena zambiri koma tidziti game inangothela pa stage p***a? ππππππΏπΏπΏπΏ
Munthu ogalukila sitimamukhulupilira
Chifukwa siku linaso azagalukila mbali Ina
Chenjelani
Muli ndi mawu otani
Kwa
Dan lu
15/09/2024
Zimene zamuonekela zonke bas nane ndasiya kuloweler mabanja ayiniake zizandiphesa akayambana uwalandisa kenako iwe uvular Iwo ndipamene akudyesana ma bisket zondipepelesa izii new song zonke umakwanaπππππ
07/09/2024
Jus Vien title chikondi changa prod by Nellie
///
Jus vien
Artist
Click here to claim your Sponsored Listing.