Avokado
Linguist| Educator| Artist| Media Mogul| Philanthropist| Events Organiser|Activist|TFD Actor|
📞Call/WhatsApp 0995057539 ( Strictly Business)
Musical Artist From Malawi.
22/06/2026
M’phunzitsi kuwupeza😆
M’phunzitsi 😆😆😆🔥
22/06/2026
Ena akuona ngati ndine Chimwendo Richard William Banda koma ayi ndithu tamgofanana😆😆
22/06/2026
Nkhope ya ndalama ilipo kale zangotsala ndi ndalamazo😆
21/06/2026
Winawake apolisi awawa atandiimitsa unakuwa kuti “chipaneni chimeneecho nchija chimakuwa mu nyimbochi!”. Apolisi ndi abale athu koma unakuwawe tisakumane😭
Men are happy people when women are not around😆🔥! Happy fathers day Anjobvu😆🔥
Ku Dowa nako. Ndinangoti “therefore”, Pano ndili kwa DC ati ndiyimire u councillor😆
Agulugufe iweyo😆🔥
Ambuye mukanandipasa voice ndi nkhope ngati Shammah Vocalz bwezi nditafa kalekale. Zikomo pondipatsa mau ngati bemberezi komanso nkhope yachonchi😭! Nyimbo ya nyuwani ya Shammah mmm🔥🔥! Link👇
Amene timakonda Karaoke, Join us again tonight at Evergreen Square. Free event 📌
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Address
Lilongwe
256