Mlangizi wachinyamata

Mlangizi wachinyamata

Share

The main aim, is to share some advise n learn more from others.

11/01/2026

Phemphero lija la ku Kapiri mu 2019 ndilo linandipangitsa kukhala Top Fan wa Rev Kambiri❤️.

Tipemphere:
Ambuye, muwakhudze anthu andale adyela awa, omwe asakaza chuma cha dziko lino.
Ambuye ayendereni anthu awa.
Ndipo pa 21 May ndipo adzaone kuthekera kwanu Ambuye.
Patsikuli mpomwe adzadziwe kuti nkhobwe si nyemba koma zangofanana mmsuzi.
Ndipo ndipomwe adzadziwe kuti opita kosiyana sapikisana.
Atate anthu awa ndipomwe adzadziwe kuti ndawala ilibe ntchito ngati wasochera.
Chauta kumwambako, anthu awa pa 21 May pano ndipomwe adzadziwe kuti msima ikalimba mkandiro sibwata.

Mumdzina lodabwitsa la Yesu, tapempha ndikusiya zonse Amen!🙏

Congratulations Rev. Kambiri. 🎉💪🔥

05/06/2025

Mkazi wakhalidwe labwino amakopa mwamuna. Ukhoza kukhala mkazi wama looks abwino, odziwa macheza akuchipinda koma ngati ulibe khalidwe uzafa uli single.
Ambuye akudalitseni abale nonse.

17/05/2025

Hello family and friends!!!

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Ntcheu?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Ntcheu