Bonkez chavula

Bonkez chavula

Share

WELCOME TO MY FACEBOOK PAGE๐Ÿ™๐Ÿ’ช
๐Ÿ’™BONKEY BONKEZ CHAVULA๐Ÿ’™โœ…โ‡๏ธ

25/06/2026

Mwamuna wanzeru amadziwa chosowa cha mkaz wake๐Ÿ˜ndipo samadikira k*ti apemphedwe kaye ayi๐Ÿ˜‹akaz ena kupempha ndikowavuta kwambr โค๏ธ๐Ÿค—

Good morning?๐ŸŒ„๐ŸŒž

24/06/2026

Girls mukazaona mamuna wangoyamba kukukondani mozipereka zaziweni k*ti ndarama zamuthera ndipo alibeso kopita kwina,koditu vamuna ndivindeletu ๐Ÿคฃ๐Ÿ™„๐Ÿ™„

23/06/2026

Mamuna wapabanja sakhala ndimzake wamkazi chimodzi modziso mkazi wapabanja sakhalaso ndi zake wamamuma umenewo ndi uhule ๐Ÿ˜…

kaya zikumvekaa? ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™

23/06/2026

Ukafuna mkazi osakonda ndalama uwumbe wako,chifukwa mkazi amafunika ndalama k*t azioneka bwino kaya tikumvana azibambo๐Ÿ‘๐Ÿฟ๐Ÿ˜„

good morning family ๐ŸŒž ๐ŸŒ…

22/06/2026

Mzimu wanga ukundiuza k*ti my future wife akufuna data ๐Ÿ˜Bea Ndilankhuleni Akhale a network yanji TNM kapena Airtel ๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚

22/06/2026

Vuto la akadzi ama hipiwa amaganiza ngati amuna tonse timawafuna, enafe timakonda mapolo amagesi omwewa๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

19/06/2026

ndikudutsa munyengo zowawa muzindipemphelerako ๐Ÿ™๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜ช๐Ÿ˜ช

14/06/2026

amuna olongosokafe sitikakamira mkazi Kungotikana kamodzi basi kamaveka๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

mwaswera bwanji! ๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…

13/06/2026

Kuli amuna andalama kunja kuno,koma sungave k*ti akwatira akaz awiri, koma winawe kungoweta abakha 4, mpaka mulu wa akaz๐Ÿคฃ

Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Upington Outlying?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Brown Street Upington
Upington Outlying
801