Project Dayfall
Back up page for Belisha fx , follow for inspiring stories
Nyimbo yoyamba
Nkhani yomwe yachitika dzulo ku mangochi kuyandikira ku admarc . Zimayi wina wapha mwana wa miyezi 4 ponena kuti sakwanitsa kumudyesa . Izi zaululika pamene apeza mwana wa mayiyu atafa ndipo zimayiyu anakumba zenje kumuikamo mwanayu Ali moyo MOTi mwana wafa chifukwa chakubanika .
Ndapeza apolisi atamunjata dzulo koma akuti mayi ameneyu ndi single mama ndipo moyo wake ndi oyendayenda choncho anthu atamupasa mimba anasiya mpaka mimba kukula mwana kubadwa ndipo wamupha mwanayo Ali ndi miyezi ingati.
Chenjezo : Chonde amalawi azanga ngati sitikwanitsa kulera mwana apaseni anthu amene angakwanitse komanso tigwritse ntchito njira zakulera kuopa zambiri.
Iyi ndi back up page ya Belisha fx pangani follow
25/05/2026
Akafukufuku apeza kuti zonse zomwe timalota ndi mbali imodzi ya mayankho azokhumba zanthu ndipo zili ndikuthekera kokwanilisidwa .
ubongo wathu umayankha zikhumbokhumbo zanthu ndichifukwa timadabwa zinthu Zina zomwe timapanga daily timazilota . Pena kulota tili olemera zimakhla kuti ife tizalemera koma timalepheretsa tokha
Basket building imaoneka ngati basket yeni yeni
Rate this song out of 10/10
I got over 10 reactions on one of my posts last week! Thanks everyone for your support! 🎉
Hi Project Dayfall
Ine ndikufuna mwamuna amene tizimvana musaike pic yanga mwamuna akapezeka timvane kuseliku .
Click here to claim your Sponsored Listing.