BrightPath Development Institute

BrightPath Development Institute

Share

We train , empower and impart knowledge. We are offering marketable diploma programs

24/11/2025

sibasi ma blesser a ku waterboard lero ndi mbiri😂

Photos from DPP Cadet's post 24/11/2025

Ma CEO onse a ma water board awatumiza kuuphunzitsi

24/11/2025

Akuti boma lapitali lidatenga TV (75) ndi galu (German shepherd) zaku State House.

koma a MCP kuba ndi izi zomwe nanga ndalama mungazisiye

24/11/2025

Kuti malawi akhale osauka chonchi wayambitsa ndi chakwera. Vuto lofanizira church ndi DZIKO

24/11/2025

Nawo a Robert Hanjahanja omwe amayang'anila Blantyre Water Board tsopano akulowera ku MUBAS kokakweza maphunzilo ngati mphunzitsi

Tilibe usilu iya

10/06/2025

Lero tinapita ku mudzi wina komwe tapeza zimayi wa ana 4 amene akuvutika kwambiri.

Ngakhale nyumba yomwe amakhala ndiyovetsa chisoni amene akufuna kuthandizapo andipanga hi ku inbox kay ndi k100 it's enough Kwa Iwo ine ndipanga zoti at least nyumb yao ndithandizepo kukonzesa . Tiyeni tithandizane

Want your school to be the top-listed School/college in Mulanje?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Address

Mulanje