Max P Spark

Max P Spark

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Max P Spark, Musician, Machinga.

12/07/2026

Senator wa United states of America wamwalira.

゚viralシ

゚viralシ

゚viralシ

10/07/2026

zathapo 🙌





゚viralシ ゚viralシfypシ゚ ゚vira

03/07/2026

ndimmene Pietermaritzburg inalili pa 30 June.

Ndikumati madhemo atendele.

03/07/2026

More than 900 arrested during South Africa’s antimigrant protests

_______________________________
Anthu opitilira 900 amangidwa Ku South Africa, kusatila ziwawa zomwe zachitika mu dzina la March and March.

02/07/2026

Zachitsoni

zinthu zafika povuta pamene abale athu ena akugona mutchire nziko la south Africa.

malingana nzomwe taona Madera a Binon nzika za nziko lino zikugona mutchire pamene zachosedwa mmanyumba komanso malo a ntchito komwe amagwila.

izi, zikuchitika mmadera osiyana siana anzikolo pamene eni nthaka ak*thamangisa nzika za maiko ena.

nao ma bwana ena nzikolo akuchosa Anthu obwela ntchito pamene Boma lawaopseza k*t akawapeza atalemba munthu obwela azilipira chindapusa cha R100,000 . ndipo eni nyumba azilipira chindapusa cha R10,000 zomwe zapeleka mantha kwawanthuwa kupangisa k*ti athamangise nzika zamaiko ena.



゚viralシ

01/07/2026

Sad news

Ngozi ya basi yomwe yachitika kunja kwa mzinda wa Musina m’chigawo cha Limpopo yapha dalaivala mmodzi pomwe anthu 11 avulala.

Basiyo inali itanyamula anthu a ku Malawi omwe alibe zikalata zovomerezeka, kupita ku malo osungirako anthu obwezedwa kwawo ku Musina.

30/06/2026

WhatsApp has announced its biggest privacy change ever: the launch of unique usernames, allowing its 3 billion users to connect and chat without revealing their phone numbers.

The Meta-owned platform said on Monday that it has begun letting users reserve unique usernames before a wider rollout later this year when people will be able to choose to be found and contacted only by their handles.

________________
Mwini wake wa WhatsApp

Walengeza kusintha kwakukulu kwambiri pa zachinsinsi (privacy), pomwe ogwiritsa ntchito ake oposa 3 biliyoni posachedwapa adzatha kugwiritsa ntchito ma username apadera polumikizana ndi kucheza popanda kuwonetsa manambala awo a foni.

Mark Zuckerberg, mwini wake walengeza k*ti kusintha kumeneku kudzayamba kugwira ntchito pang’onopang’ono, ndipo cholinga chake ndi kupititsa patsogolo chitetezo ndi kusunga zinsinsi za ogwiritsa ntchito a WhatsApp.

Iye anati ogwiritsa ntchito adzatha kusankha ma username awo apadera, zomwe zidzawathandiza kulumikizana mosavuta komanso motetezeka popanda kugawana nambala ya foni. Kusinthaku kukuyembekezeka kufika kwa ogwiritsa ntchito ambiri kumapeto kwa chaka chino.

゚viralシfypシ゚

゚viralシ

30/06/2026

Phakela mnthakati ndi nzake ngizwe chunu, anayitanidwa kwa president Cyril ramaphosa.

Anyamata a gulu la March on March aitanidwa ndi Purezidenti Cyril Ramaphosa ku msonkhano wapadera pa Lolemba, 29 June 2026, k*ti akambirane madandaulo awo okhudza nkhani ya kusamuka kwa anthu komanso alendo osaloledwa kukhala m’dziko.
Pamsonkhanowu, Purezidenti anawauza k*ti ngakhale nzika zili ndi ufulu wochita zionetsero, ufulu umenewo uyenera kuyendera limodzi ndi udindo wotsatira malamulo komanso kusunga mtendere.
Anapitilizanso kunena k*ti boma likugwira ntchito pothana ndi nkhani ya migration, ndipo boma lokha ndi lomwe lili ndi mphamvu zokhazikitsa ndi kukakamiza malamulo okhudza anthu olowa ndi kukhala m’dziko.
Purezidenti anapemphanso onse omwe akuchita zionetsero k*ti azichita mwamtendere komanso motsatira malamulo a dziko.

23/06/2026

Boma likupereka ndalama kwa aliyense k*ti akwelere kupita kumudzi kwao. Apafupi akupatsidwa MK70,000. Uyu amubela yonse amapita ku Mangochi.
Wangokhala ku stadium k*thedwa nzeru.

Kumasamala ndalama Koma nthawi zonse akuakulu.

゚viralシfypシ゚
゚viralシ

23/06/2026

The Thom Mpinganjira family has donated K100 million to the Malawi Government through Dodma to support the repatriation of Malawians affected by anti-immigrant attacks in South Africa, saying no Malawian should be abandoned during a crisis.

Wakulu Thomson Mpinganjila watenga nawo gawo posamutsa anthu omwe ali pachiopsezo dziko la South Africa.

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Machinga?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Address

Machinga
98

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Max P Spark posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Subscribe

We will notify you when anything happens in Machinga.