Mpanjee Buzz
entertainment is life
21/06/2025
Upcoming artist uyuyu Chap Magang akubwera ndi mkokomo ngati cyclone Fred. Mpaka kuimba ndi Winter Charge π₯πwhat a big feature. Koma Khili alimo umu? Winter sayendatu yekha.
yakumana ππ₯π₯
now in different websites.
Predictions on Mpanjee Buzz page. Kapangeni predict kumeneko!
Airtel sem final,
Bullets vs karonga United
21/06/2025
Apopo atangolandira message yoti " I am coming over for Netflix and chill" mmene ingasinthire room yoπππ.
Boys can relate, mesa Anzanga otayiriraπ
Kodi why do we put drama paliponse πππ komanso if you check, gender ina ija palibepotu apaπππ
Azimayi atimaliza sure eeehπππ
Ati mukanabwera ndi nkhunituπππ
Rise and shine! Saturday is God's invitation to rest, recharge, and rejoice in His creation.
Happy Sabbath
Pavute pasavute tiphula π€! Tipanga zotheka basi
Kumaona ziweto zopitisa ku lobola π
20/06/2025
Kumasamalila tsitsi bwino bwino ehe
19/06/2025
Tingojambula kuti mwina zichuluke π
Crispy wapeza abale π
Click here to claim your Sponsored Listing.