ANEBA
CHILUNGAMO🙄🤲🇲🇼🤸♀️🤸♀️🤩😏
With ChiQuo The-Alien – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!
Nde kuli uyu mumamuti apolo yu, asaaah pansana pako weduro 😂🙌😂
08/04/2026
BREAKING NEWS🔥OLAKWA NDANI😭
Anthu ambili akufusa kuti Kodi Steve chinga wayamba chamba kapena ndi Misala...abare nkhani ndiyoti Steve wati "Mayi ake sadabwedwe ndi Bushili monga momwe akunenela Peter sambo...koma Mayi ake adamwalila atadwala kwa nthawi yochepa
Ndeno fuso likuti atamwalila iwo omwewo adatulusa kalata yomwe ankati adasiya mayi awoo...Kodi kalata inkati chanii ???? nanga Bwanji kare lonse lija Bwanji sadanene kuti mayi awoo anadwala kwa nthawi yochepa???
According to you apa nkhani mwaiva Bwanji Steve walankhula bwino kapena akudziwapo kanthu nayeso..😭 Rip Grace chinga
08/04/2026
pop young wakhumudwa kwambili akufunika chithandizo mwanayu
For the past 3 years as an independent artist, I have learned so many things.
1. People think that if you are independent, you are useless.
2. Every project you drop becomes “useless” in people’s eyes.
3. They wait for your downfall, not your progress.
4. You become a topic, kuti pano sangapange zolongosoka coz he is alone.
07/02/2026
fada ChiQuo The-Alien kudzangotulukila
https://youtu.be/gprNTX3Md4w?si=sPpG4smulFYjbC4y
27/01/2026
A polisi ku Blantyre amanga Charlotte Botha wa zaka 20, kamba komuganizira kuti amabera anthu ndalama pa masamba a mchezo a Whatsapp ndi Tik-Tok.
Wachiwiri kwa mneneri wa a polisi ku Blantyre, a Dorris Mwitha, wauza VEGAH REAL kuti, Charlote amauzanso anthu otchuka omwe ena amayenda nawo kuti amupatse ndalama ndipo akapanda kutero awayalutsa.
A Mwitha ati mayiyu amanamizanso anthu kuti amagwira ntchito ku tsamba la mchezo la Mikozi kuti anthu awope ndi kupereka ndalama msanga.
💔😅
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Lilongwe