OH Yeah

OH Yeah

Share

Welcome to Official page of [Oh Yeah]
For Entertainment, Education,
Exploring the Country(Malawi),
Sharing thoughts. Connecting People. CEO Chavula Nicklaus

promoting Music, Movie and Poems. RUTHLESS IDEALISTIC

08/04/2026

Hello Family
Avoid a partner who will put their friends before you.. it'll never work out

08/01/2026

Zimakhala zowawa kufusira Maid nde akukaneso mu nyumba yako yomwe

04/01/2026

Koma chipanda Mulungu ndi Nyimbo bwezi tili ndani?😪

04/10/2025

Mwandisowa

Mwakhaula akuyakhula mu khani iyi ndan 😂😂😂🙌

04/07/2025

Opulumutsa(rescuers) ku Indonesia akufufuza anthu ambiri omwe asowa atamira pa boti pafupi ndi Bali .

Gilimanuk, Indonesia AP - Opulumutsa ku Indonesia anali kufunafuna anthu 29 omwe adasowa Lachinayi pambuyo pa boti litamira ndipo anthu asanu ndi mmodzi(6) adamwalira usiku watha pafupi ndi chilumba cha Bali ku Indonesia.

Mnyamata wazaka zitatu ndi amayi ake ndi omwe anafera pafupi kwambiri omwe matupi awo adachotsedwa dzuro Lachinayi masana. Matupi 6 omwe apezeka aja atengedwera ku mabanja awo ku Banyuwangi, akuluakulu aboma adatero.

Munali anthu 53
Anthu 30 Ali safe apulumusidwa
Anthu 6 apezeka atafa
Meaning while anthu 17 sanapezeke

Follow Malawi VLOG for more news and entertainment

28/06/2025

Your girlfriend looking at you because you're watching Super League matches at a time she is supposed to be watching ZeeWorld movies.

Good morning Neba 🤣

Want your business to be the top-listed Media Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address

Dungeness Rd, Romney Marsh TN29 9NB
Lilongwe
TN29 9NB