Frend
Reminding the ummah all praise is due to Allah who teaches a person things he doesn't know..
01/06/2026
Osamuka! Osamuka! aiwala ujeni padenga🤣🤣
09/05/2026
Ndi kangati ndakhala ndukuuzani kuti follow Frend ndi mfana wa bho koma inu simufuna kutsatira ayi, taonani mwasemphana ndi ma update abwino ndipo simudzawaonaso kufikira mutatsatira iye.
😁😁
06/05/2026
Akumati ndi ma graduate.
Alinawotu ma degree.
Amati ndi ophunzira iwowo.
Chipanda chodzadza ndi utoto wa maphunziro adamwera iwowo.
Amati ndi ozindikiratu iwowo.
Anawerengatu ma book ochuluka.
Amadziwa zinthu zosiyanasiyana.
Koma zoti chisilamu n'chipembedzo monga chilichonse.
Si chilankhuro komaso mtundu wa munthu.
Koma n'chipembedzo cha aliyense.
Sadziwatu iwowo.
Aliyense ooneka mwa chiluya.
Ooneka mwa chimwenye ndinso mwa chiyao.
Okhala nalo dzina lomveka mwa chiluya.
Olankhura chiluya ndinso chiyao.
Ameneyotu ndi msilamu kwa iwowo.
Zoti Arabic ndinso chiyao.
Ndichilankhuro monga chingerezi, chipwitikizi ndinso chichewa.
Sadziwatu iwowo.
Komatu iwowo, amati ndi ophunzira.
Amati ndi ozindikiratu iwowo..... .............to be continued
Rafiq Saidi Assami
MAV TALK SHOW
Indee Voices
Hûssêíñ Mâílôs
Brown Chrispine
04/05/2026
KAMOYO KA THANZI NDINKANYADIRA KAJA LERO KULIBE.
NDANGOTSALATU MAFUPA NDIMMENE UKUNDIONERAMU.
KUCHIPATALA NDIINE KABWEREBWERE
BWEZI LA MPHASA NDIINE NDILI PANO.
NDAYESAKO MAKHWALA ACHIKUDA.
MPHINI NDI IZI ZIKUCHITA KUWALA KAMBA KOBWEREZA.
ASING'ANGA AMIZIMU MA SHEHE A MATALAZIMU, OSEWO NDAWAYENDERADI SINDINGAKANE........
PEPA!! PEPA!!....
01/05/2026
Uku nde kuipitsirana mbiri uku iih😂🙌
Mwawina 12:0
ehee mnyamata Ali chinthuzi akuoneka Kuti akhoza kutitutumusa ndi chi ndakatulo chabho Chaka chino
Ife kwanthu Ku ya ng'anira kunjira iwe rafiq saidi Rafiq Saidi Assami
tavumbuluka !!!!
14/04/2026
Zikomo kwambiri KUMPANDO mnyamata uja zuchitika kunooooo😊😊😋
MOSAKAIKA UDZAFA KUMANDA TIDZAKAIKA.
💯
Ineyo nduona ngati mnyamatayu za ma nasheed zija zinkamuchedwetsa, inu muona bwa? 🤣
Omar Ussi zabho?
FROM TUBING TO WIRING AND ALL ELECTRICAL SOLUTIONS – WE'VE GOT YOU COVERED! ☂️
🤙 CONTACT US TODAY FOR EXPERT SERVICE AND RELIABLE SOLUTIONS.
Cell: 0880110174/0996143927 | Lilongwe
OMAR ELECTRICALS!! OMAR ELECTRICALS!!
_Electrifying your world safely_ 💡
NDINGO UJENI PANG'ONO.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Address
Lilongwe