Samp Engineering

Samp Engineering

Share

We offer
⚙️ Industrial machine maintenance and service
⚙️ Industrial machine Installation
⚙️ Welding and fabrication

25/05/2026

Meet my friend,Dylo Sidesi...

Mfana opusha ngini,wa masomphenya 🤝🛠️

19/05/2026

Confined space.

Today's topic.

Kodi munanvako za mawu oti confined space?

Awa ndi Malo omwe amakhala okwana thupi la munthu koma mokakamizikako... Dziwani kuti Malo amenewa amakhala ndi mlingo ochepa wa mphweya, omwe timapuma(Oxygen)..

Ziopsezo zake:

1.Kutentha kopyora muyezo.
2.kuchepa Kwa mphweya wa oxygen.
3.Kutelera ngati malowo panali za madzimadzi.
4.kuomba Khomo mosakonzekela.
5.kuyendesedwa ngati sitinapange Isolate.

Izi ndi zina mwa ziopsezo za Confined space.

Ndondomeko za kagwilidwe ntchito mu confined space.

1.Onesesani kuti mulibe vuto lakapumidwe pa nokha.

2.Onesesani kuti Malo omwe mugwile ntchito wo mwawaona bwino bwino. Ndipo Mwapanga sign Work permit,

3.Onesesani kuti a safety a pa company panupo akudziwa za pomwe inuyo mukugwilira ntchito, ndipo akupasani munthu okuyang'anilani.

Note: Munthu okuyang'anilani pomwe muli mu confined space Akhale odziwa ntchito yake,yopulumusa anthu, osati kungoti Bola Pali Munthu,

4.Ngati kupuma nkovuta Kwambili Ku malowo, onesesani kuti pali zipangizo zothandizila kupuma..

Supervisor wanu ndi udindo wake kumakuyendelani pafupi pafupi kuti aziziwa za mmene ntchito ikuyendela.

18/05/2026

What is a confined space? Another lesson is coming!

Follow 👉 Samp Engineering for more Mechanical engineering lessons.

18/05/2026

Kodi malamulo a working at height Ku ntchito kwanuko amatsatidwa? 🤨... Musafele ntchito,. Comment section muli ndondomeko zonse. 👇🤝

18/05/2026

ME Students tell us, what are these guys 👇

08/05/2026

Happy weekend! Remember to attend Church services..

Want your business to be the top-listed Equipment Service in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Website

Address

Kanengo
Lilongwe