Wizzy p

Wizzy p

Share

Dancell founder

Dan Sanudi x Hussein Banda -Ukamapita 20/03/2026

nthawi zina moyowu umatipusitsa eeeeeeπŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’” nyimbo iyi ya (ukamapita) yandikumbutsa zakale ndipo ndalila iwoneleni mukatha kuwonela mudziwuza.

Dan Sanudi x Hussein Banda -Ukamapita This song expresses the feeling of hearts as Ramadhan comes to an end and what transpires thereafter.written and performed by Da...

12/03/2026

pano temwa akungotulutsa ma pic uyutu adavaya

12/03/2026

RIP DEE TRICE ukapelekeko moni kwa martseπŸ˜­πŸ˜­πŸ’”

12/03/2026

muli mbali iti
USA
IRAN

09/03/2026

komatu guys mmmmhhhh

12/02/2026

ndi angati amene mwasangalala kuchoka kwa zaka pa social media?

16/01/2026

uhule ndi ntima osati mavuto kuli anthu ambili mdziko muno amene akuvutika koma simahule, uyuyu thandizo loyambilila amafunikila kumapemphero k*t chi chiwanda cha uhulecho chikachoke then ndikumuthandiza bwino ku mbali yazachuma koma olo mutamupatsa ndalama zochuluka bwanji popanda mwini wakeyo kulapa kusiya tchimo sangasiye uhule adzikapangabe koma ali ndi ndalama.

06/01/2026

inu muli mbali itiyo?

28/12/2025

eli njuchi macheza anu akumadzatibalalitsaso wezi πŸ˜€

09/11/2025

yowina ndima bankers koma akusangalala ndi a buletsi

07/11/2025

star

07/11/2025

mawu amodzi kwama guys awa

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Lilongwe