Max Complex

Max Complex

Share

FOR AFFORDABLE PRICES

Photos from Max Complex's post 14/04/2026

Mukufuna chiyani chomwe ku Max Complex kulibe,,

Ndalama yanuyo ndi yanu basi,, mukapanda muigwiritsa ntchito mosamala, muvutike ndi nokha basi,,

Musazaname kuti simunauzidwe..

Earn once, Spend Once only at MAX COMPLEX ❤️❤️

Photos from Max Complex's post 14/04/2026

Tayambo,, Nsinjiro zongophula kumene,, Max Complex siimaphweketsa

Zotchipa as always
Earn once, Spend Once❤️

25/03/2026

NTHAWI ZINA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..

KU Max Complex NDI MALO OKHAWO AMENE MUNGAGULE KATUNDU WABWINO PA MITENGO YABWINO..

LILOLENI BANJA LANU KUTI LIYAMBE KUDYA MPUNGA POGULA KU MAX COMPLEX,, MUKAGULA KWINAKO,, MUMAONA NGATI MUKUGULA MPUNGA KOMA USALI MPUNGA INU NDIKUMANGODABWA KUTI MPUNGA WANJI OPANDA PFUNGO,, PENA KUMAONA NGATI VUTO NDI AMAYI MAPHIKIDWE..

MUKATERO AMAYI KOMANSO ANA ANU AZAKUDANDAULANI MOYO WAO ONSE..

YAMBANI KUPANGA ZIGANIZO NGATI MUTU WA BANJA POGULA KATUNDU WABWINO KU MAX COMPLEX

TIPEZENI KU AREA 23 ALONG KAMUZU BARRACKS TARMAC ROAD NEAR KACHERE CCAP 🔥🔥🔥💯💪

25/03/2026

PENA UMAZAONA NGATI VUTO NDI MADAM KOMA VUTO LIRI LANU KAMBA KOMANGOGULA ZINTHU MALO OSADZIWIKA BWINO..

KU Max Complex NDI KU MALO KUMENE MUNGAPEZE KATUNDU WABWINO PA MITENGO YABWINO..

UKAKHALA MPUNGA NDIYE NON CAN BEAT US.

LILOLENI BANJA LANU KUTI LIYAMBE KUDYA MPUNGA POGULA KU MAX COMPLEX..
UDINDO OSAMALIRA BANJA LANU, ULI MMANJA MWANU..
MUSALIDYETSE BANJA LANU ZINTHU ZOONEKA NGATI MPUNGA KOMA USALI MPUNGA,, MKAZI KOMANSO ANA ANU AZAKUDANDAULANI MOYO WAO ONSE..

YAMBANI KUPANGA ZIGANIZO NGATI MUTU WA BANJA..

TIPEZENI KU AREA 23 ALONG KAMUZU BARRACKS TARMAC ROAD NEAR KACHERE CCAP

25/03/2026

MAX COMPLEX IS NO JUST A NAME

IT'S A BRAND THAT SELLS ORIGINAL COMMODITIES AT A FAIR PRICE

ORIGINAL BIC PEN MK700

PUROLA 2 litre MK15,000

SUPER MAHEU MK2,000

NICE ONE. MK2,000

SOBO 2 litres MK11,000

GLAM & GLORY (SNAIL WHITE LOTION). MK3,500

MOVIT BABY JELLY 200g MK6,500

MPUNGA WA KILOMBERO MK4,000 Per kg

MAZIRA. MK12,000 PER TRAY

TOP SOCIETY BABY JELLY 500g MK12,000

CERELAC Regular MK10,000

BOTSALT 500g MK1,000

SOFTCARE PAMPAZ MK10,000 Pack of 25

And many more including spices like Raja, Garlic powder, Tumeric powder, paprika powder etc

Come and Visit us in Area 23 along the Kamuzu Barracks Tarmac Road near Kachere CCAP or visit Maxcomplex on Google maps

13/02/2026

Mpunga timapezeka ndi Kilombero wabwino kwambiri at a Fair Price

MK4000 per kg only

21/01/2026

Affordable prices always

03/11/2025

Affordable Prices 🙆

Johnson baby jelly MK14,000
Top Society baby jelly MK12,000
Ingrams MK14, 000
Vestline 120grams ,,MK2,500

25/10/2025
07/03/2025

HOPE brings SUCCESS 💪

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Kamuzu Barracks Tarmac Road
Lilongwe

Opening Hours

Monday 06:00 - 21:00
Tuesday 06:00 - 21:00
Wednesday 06:00 - 21:00
Thursday 06:00 - 21:00
Friday 06:00 - 21:00
Saturday 06:00 - 21:00
Sunday 06:00 - 21:00