MAIZE Farming Project

MAIZE Farming Project

Share

Let us end Malnutrition, poverty, hunger and create more job opportunities, innovating and executing ideas from the word of ideas into the real world.

08/06/2025

MBIRI YA RALPH KASAMBALA.

Lero tatiyeni tive mbiri ya Ralph Kasambala yemwe adatisiya tsiku ngati la lero pa 7 June chaka chatha.

Ralphael ndiye dzina lake limene makolo ake mai ndi bambo Kasambala adamupatsa atangobadwa, koma adalidula dzinali ndipo amangoziwika ndi dzina loti Ralph.

Ralph adabadwa pa 26 September 1969 m'boma la Nkhata Bay limene ndi boma lomwe limapezeka kumpoto chakumawa kwa dziko la Malawi.

Ralph adali wa ntundu wa chi-Tonga komaso wa chipembedzo cha chi-khristu ndipo amapemphera mpingo wa Roman Catholic RC.

Atamaliza maphuziro ake a pulayimale komaso sekondale adakachita maphuziro ake a za malamulo ku Sukulu ya ukachenjede ku Chancellor College.
Kumeneko adatenga tsamba lake la Masters degree za malamulo.


Ralph Kasambala adagwira ntchito monga m'phuzitsi ku Sukulu ya akachenjede ya Chancellor College (University of Malawi).

Adakhalaso mkulu wa bungwe la Malawi Law Society kuyambira mu chaka cha 2003 mpaka 2004.

Ralph Kasambala adasankhidwaso ndi Dr Bingu Muthalika ngati mlangizi wa boma pa nkhani za malamulo iyi idali term yoyamba ya Bingu Muthalika.

Ralph adayimiriraposo milandu anthu odziwika bwino monga Dr Joice Banda pa mlandu omwe sadavane ndi Dr Bingu Muthalika.
Kasambala adagwiraso ngati Lawyer wa mtsogoleri wa dziko la Zambia a Micheel Sata.

Pa 26 April 2012 Dr Joice Banda adasankha a Ralph Kasambala kukhala nduna ya za chilungamo komaso nthawi yomweyi amagwira ntchito ngati mlangizi wa boma pa nkhani za malamulo, koma adadzachotsedwa pa 10 October 2013 pomwe Dr Joice adasankha nduna za tsopano.

Kupatula zimene zimenezi Ralph adayimirira anthu osiyanasiyana pa Milandu.


Ralph Kasambala adamangidwapo pa chifukwa cholimbana ndi boma la Bingu ndipo umu mudali mu February 2012.

Pa 8 November 2013 Ralph Kasambala adatsiridwaso unyolo pa nkhani yokhudza kuba ndalama za boma zija zimangodziwika kuti Cashgate komaso mlandu okoza chiwembu chomofuna kuppha a Paul Mphwiyo.

Adakhala m'manja mwa police k

22/02/2025
09/02/2025

LETS CREATE MORE JOB OPPORTUNITIES, END HUNGER AND MALNUTRITION, POVERTY AND ADOPT FRIENDLY FARMING PRACTICES TO OUR OWN COUNTRY AND ACROSS THE BODER.

06/02/2025

LETS END MALNUTRITION, HUNGER AND POVERTY.

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

P. O BOX 2218, BLANTYRE
Blantyre