PEMU
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from PEMU, Musician/Band, Blantyre, Blantyre.
Nthambi yowona za nyengo yati kukhalabe kopanda mvula kwa masiku opitilira sabata limodzi m'maboma a chigawo cha kumwera zomwe zidzetse ng'amba.
Malinga ndi uthenga omwe nthambiyi yatulutsa lero, maboma omwe akhudzidwe ndi vutoli ndi monga; Chikwawa, Nsanje, Blantyre, Thyolo, Mwanza, Neno, Zomba, Phalombe, Mulanje, Balaka, Machinga, ndi Mangochi.
Nthambiyi yati maboma ena a chigawo chapakati monga; Salima, Dedza, Ntcheu, Lilongwe Mchinji, Dowa ndi Ntchisi akhudzidwanso ndi vutoli.
26/01/2026
Malinga ndi malipoti awa ndi bambo Kamanga ndipo amakhala kwa Chinsapo ku Lilongwe.
Dzulo anapita Ku toilet kuti akazithandize (toilet yokumba) nthawi inali m'ma 6 kenako akuti sanabwererenso.
Kuwasakasaka anapezeka chamma 9 usiku ataguvukila mu toilet yokumba.
Anyamata anagwila ntchito mwachangu-changu yofukula chimbudzichi mwatsoka anapeza bambo Kamanga atafa kale nsambi abale zokhudza kwambili.
Mzimu wawo uuse muntendere.
25/01/2026
SADNEWS 💔 chithunzichi chikuwonetsa Moses John, amene zikumveka zoti wachita kuphedwa.
Moses anali wokhala ku Mtandire, Area 56 ku Lilongwe, ndipo ankapeza moyo wake pogwira ntchito ya kabaza, kunyamula anthu kuchokera kumalo ena kupita kwina ndi kulipidwa.
Anapezeka atamwalira m’dera la Airwing, ali ndi mabala angapo a mpeni. Njinga yake ya kabaza komanso nsapato zake zinabedwa ndi anthu amene anamupha, omwe mpaka pano sakudziwika.
Moses ayikidwa maliro lero, pamene abale, anzake, komanso anzake a ntchito ya kabaza akulira imfa ya mnyamata wolimbikira ntchito, yemwe moyo wake wathera mwankhanza kwambiri.
REST IN PEACE MOSE🕊️🕊️🕊️
24/01/2026
Kunali Social Weekend ku Holy Family College of Health sciences “Phalombe”…koma ayi zikomo
23/01/2026
Amasenda Galu kuti azigulitsa, eya mang'ina omwewa.
Anthu amugwira😂💔😭😭
07/01/2026
Company ya Goshen City yomwe imasogoleledwa ndi Prophet Sheppard Bushiri yathetsa mgwirizano wawo ndi Bungwe la Film Association of Malawi lomwe wapampando wake ndi Dorothy Kingston mgwirizanowu watha
29/12/2025
Hon. Richard Chimwendo Banda atuluka mchipatala komwe anawagoneka akudwala msana ndipo awatengela Ku Ndende ya Maula kuti azikadikilila kumeneko.
Chimwendo akuganiziridwa kuti amafuna kupha munthu mu 2021
26/12/2025
Eli Njuchi Cancels The Hive Experience show which was scheduled for tomorrow following the tragic accident involving his band members.
May Souls of those lost rest in peace 🕊️
22/12/2025
Chichokeni ku Phalombe pa 24th November kupita ku Lilongwe sadafikebe [ MISSING FOR 1 MONTH 📥 ]
Mayi Patience Nangwale ndi mwanayu Madalitso adanyamuka pa 24th November kumabwela ku Lilongwe kuno. Kulankhula nawo komaliza panali pa 24th November pompo ankati akudutsa Zomba kungochoka pamenepo adachoka pa line kufikila lero 22nd December sanafike.
Chonde amene angawawone anene ku police or call 0999912701 / +265 994 69 79 93 / 0992225350
Please please please
manizo wabwela Manizo Agena
18/12/2025
🚨 Mulandu wa Vj Ken ukhala ukulowaso khothi Mawa.
Mwazina Mulandu umnewu unaimitsidwa pamene anapeleka Bail komanso kuti Boma lipeze Mboni zogwirika Pa Mulandu umene akumuganizila Vj Ken kuti angona Ndi Mwana wazaka 15.
18/12/2025
Patapita 3 weeks Beatrice Chabwera (21) chiphedwereni ku Lilongwe, Rodwell Lumbe akulondoloza za imfa yake patakambidwa zambirimbiri m'masamba amchezo.
Lero 7pm aulutsa program imene wayankhula ndi anzake a Beatrice, mayi ake, abwana ake, komanso apolice amene akuyendetsa nkhaniyi.
Adali ndindani Beatrice usiku umene anaphedwa?
Anzake, abwana ake, komanso Mayi ake akutipo chani?
Nanga a police akutibwanji?
Wasiya kamwana ka zaka zitatu, aMalawi tingamuthandize motani?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Culinary Team
Attire
Address
Blantyre
0000